Anatchezera
Takulandiraninso mu 2021 Ndikufuna ndikulandireni m’chaka cha 2021. Chaka chatha lidali thumba la zambiri. M’chakachi zina zidali zokoma, koma zina...
Takulandiraninso mu 2021 Ndikufuna ndikulandireni m’chaka cha 2021. Chaka chatha lidali thumba la zambiri. M’chakachi zina zidali zokoma, koma zina...
Akukana banja Gogo, Ndidapalana ubwenzi ndi mtsikana wina chaka chatha. Ndimtsikana wokongola, komanso waulemu. Chomwe chimandidabwita n’choti ndikamuuza zabanja amakana....
Ndili pa moto Gogo, Ndili pa ubwenzi ndi mtsikana wina yemwe amaphunzitsa pa sukulu ina ya pulayimale ya mu mzinda...
Gogo, Ndili pa banja ndipo tili ndi mwana mmodzi. Koma vuto ndi loti anthu anawanamiza amuna anga kuti ndili ndi...
Akufuna mwana Gogo, Ndakhala m’banja ndi mwamuna wanga zaka zisanu, koma wopanda mwana. Mwamuna wanga amalimbitsa mtima kuti ndisadandaule popeza...
Agogo ndili ndi zibwenzi ziwiri koma onsewo ndi pachibale komanso amadziwana. Ndikawauza kuti andisiye onse amakana, nditani gogo chifukwa onse...
Akufuna mwana Gogo, Ndakhala m’banja ndi mwamuna wanga zaka zisanu, koma wopanda mwana. Mwamuna wanga amalimbitsa mtima kuti ndisadandaule popeza...
Ndipite kwa asing’anga? Zikomo Anatchereza, Palitu mkazi amene amandizunguza bongo. Mtima wanga nthawi zonse umakhala pa iye ndipo sindigona tulo...
Akufuna mwana Gogo, Ndakhala m’banja ndi mwamuna wanga zaka zisanu, koma wopanda mwana. Mwamuna wanga amalimbitsa mtima kuti ndisadandaule popeza...
Sakufuna kukaonekera Gogo Natchereza, Mnyamata wina adandifunsira chibwenzi ndi cholinga choti tidzakwatirane. Padakali pano padutsa zaka zinayi tili paubwenzi, koma...
Sakufuna kukaonekera Gogo Natchereza, Mnyamata wina adandifunsira chibwenzi ndi cholinga choti tidzakwatirane. Padakali pano padutsa zaka zinayi tili paubwenzi, koma...
Kodi nditani? Gogo Natchereza Ndine mtsikana wa zaka 25 ndipo ndakhala pa chibwenzi ndi mnyamata wina kwa zaka zinayi. Mnyamatayu...
Akundidabwitsa Anatchereza, Ndili pa chibwenzi ndi mwamuna wina. Chomwe chimandidabwitsa n’choti nthawi zonse ndikamuimbira foni usiku samayankha. Ndikamufunsa amati idali...
Ndikufuna kuchoka Zikomo Anatchereza, Ndidabwera kutauni kudzafuna ntchito ndipo ndidasiya mkazi wanga kumudzi. Ntchito ndidaipeza koma abale amene ndimakhala m’nyumba...
Ukuchita njomba Gogo Natcheteza, Ndine mtsikana wa zaka 25 ndipo ndakhala pa chibwenzi ndi mnyamata wina kwa zaka zinayi. Mnyamatayu...
Akundifunanso Anatchereza, Telemu yotsiriza ya Fomu 3 ndidapalana ubwenzi ndi mtsikana wina pasukulu yathu ku Mulanje. Koma tikuyandikira kulemba mayeso...
Adandichotsa ntchito Zikomo Gogo Ndakhala ndikugwira ntchito kwa bwana wina mumzinda wa Blantyre kwa zaka 4. Masiku apitawa ndidaapempha holide...
Mkazi wanga koma mkonono Agogo, Langa ndi dandaulo pa mkazi wanga wokondeka. Iyetu mwano alibe ndiponso ntchito amagwira molimbika. Abale...
Akunyengana ndi mnzanga Zikomo Anatchereza, Ndakhala pabanja zaka 7 ndipo tilinso ndi mwana wa zaka 7. Tsiku lina mwanayo adathyoka...
ANATCHEREZA Akundikakamira Ndili ndi mkazi yemwe ndili naye mwana mmodzi. Vuto lake ndi limodzi: amakhalira kunyoza makolo ndi abale anga....