Ref speaks out on Airtel Top 8 final

  Referee Micheck Juba who officiated the Airtel Top 8 final between Nyasa Big Bullets and Blue Eagles which was marred by violence, has come out of his shell to defend his decision to award Eagles a late penalty. Juba was physically confronted by Bullets fans and players after the match for awarding Eagles a…

Kamuzu Stadium gets fresh deadline

  Government and contractors responsible for Kamuzu Stadium renovations in Blantyre have set July 30 as a deadline to have the works completed and hand over the facility to the Ministry of Labour, Youth, Sports and Manpower Development. This follows a visit to the stadium by the ministry’s director of sports Jameson Ndalama yesterday which…

La 40 lakwana kwa womata anthu phula

Wakhala akumata anthu phula m’midzi kuti amupatse ndalama ndipo adzakhala ndi mwayi wopeza ngongole kuchokera ku bungwe la Emmanuel International. Midzi 21 ya kwa gulupu Makumba ndi Mtaka ikulirira ku utsi atawakwangwanula ndalama dzuwa lili gee! La 40 lamukwanira Wyson Mandolo wa zaka 36 pamene bwalo la milandu m’boma la Mangochi lamupeza wolakwa ndipo akukaseweza…

‘Zovota ife ayi’

“Anthu opotsa 3 000 adalembetsa unzika m’dera langa. Lero anthu 1 240 okha ndiwo alembetsa kalembera wa zisankho.” Izi ndizo zachitika m’dera la mfumu Chilowamatambe ku Kasungu komwe bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) limachititsa kalembera wa zisankho moti likapanda kubwererako, anthu ambiri sadzavota nawo m’bomalo pa zisankho zapatatu za chaka cha mawa. “Anthu akuti…

Kampeni yayamba ndi ukali

DPP ithamangitsa otsutsa ku Thyolo Kumeneko ndi kunyumba kwa APM—Chakale Kwa eni kulibe mkuwe. Mdima udadza masanasana m’boma la Thyolo pamene gulu la Chilima Movement lidalephera kuchititsa msonkhano wake nkhondo ya mawu itabuka ndi otsatira chipani cha DPP. Wachiwiri kwa mlembi wa DPP, Zelia Chakale, adati gulu la Chilima Movement lidachita kuishosha dala chifukwa limafuna…

Kalembera wa zisankho ali mkati

Dzuwa salozerana, kalembera wa zisankho udayamba Lachiwiri m’maboma a Dedza, Salima ndi Kasungu. Izitu zikudza pokonzekera chisankho cha makhansala, aphungu a Nyumba ya Malamulo ndi mtsogoleri wa dziko lino chomwe chidzachitike mu May chaka chamawa. Aliyense ali ndi mwayi wodzavota akalembetsa. Kutanthauza kuti ngati munthu salembetsa, sadzapeza mwayi wodzaponya nawo mavoti. Komishona wa bungwe loyendetsa…

Gulewamkulu, agumula sitolo

Gulewamkulu wina Lachwiri lapitalo akumukayikira kuti adagumula sitolo ina pamsika wa Nkhalambayasamba m’boma la Mchinji ndipo akumukaikira kuti adasakaza katundu wa K3.5 miliyoni. Mneneri wapolisiyo, Kaitano Lubrino, Lachisanu adati apolisi amanga anthu 16 amene akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi nkhaniyo. “Anthu onsewa tikuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi zophwanya sitoloyo komanso kuba katundu,” adatero Lubrino. Malinga ndi Lubrino,…

Milk wastage to drop

The country will start registering a drop in milk wastage following the opening of K1.5 billion milk collecting centre and cooling plant by Lilongwe Dairy Limited at Goliati in Thyolo. Over the years, milk wastage has been a key issue for bulking groups due to unpredictable power supply and poor maintenance of collecting plants. The…

Mangani womenya wotsatira MCP

Chipani chotsutsa cha MCP chapempha apolisi kuti aponye m’chitokosi Isaac Jomo Osman, kadeti wa DPP amene adasautsa ndi kuvulitsa mnyamata amene adavala malaya a chipani chotsutsacho. Lachiwiri m’sabatayi, Osman, yemwe adakhalapo wapampando wa masapota a Big Bullets, adajambulidwa akulamula mnyamatayo amene adavala malaya a makaka a MCP kuti ‘avule ndipo asadzayerekeze kuvala makakawo.’ Izi zidachitika…

Chilima saima nawo

Uli dere n’kulinga utayenda naye. Amene akufuna kuti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima adzaimire chipanicho pachisankho cha 2019, ati sakutekeseka ndi ganizo lake lofuna kusamuka m’chipani komanso kukana kukapikisa nawo kumsonkhano waukulu. Lachitatu, Chilima adabwera poyera koyamba chibadwireni mpungwepungwe m’chipani cha DPP kunena kuti iye sakapikisana nawo pa msonkhano waukulu womwe uchitike…

Drug resistant TB patients face expulsions

Our Staff Reporter exposes how a group village head expelled her daughter-in-law, a glimpse of discrimination and exclusion of people with multidrug-resistant tuberculosis (MDR-TB). She wanted a happy marriage, but Esther Loleya’s dream was shattered when her mother-in-law sent her packing. The 33-year-old was forced to separate from her husband of three years after being…

Mswahara wa zifukwa

Munga wadza ndi mafinya omwe. Pamene ena akumwetulira kuti boma lakweza mswahara wa mafumu, mafumu ena ati kukwezaku kuwabweretsera mavuto pa ufumu wawo komanso ku boma. Ndondomeko ya zachuma yomwe nduna ya zachuma yabweretsa, boma lati likweza malipiro a mafumu ndi 100 pelesenti ngati aphungu avomereze bajeti imene nduna ya zachuma Goodall Gondwe idapereka m’Nyumba…

Chande says not going back to Nomads

Be Forward Wanderers striker Jaffalie Chande has said he is not going back to the TNM Super League champions. The wayward striker’s latest upshot comes after Wanderers chairperson Gift Mkandawire said last week the team was in talks with the player on his return. “Me, playing for Wanderers? No! That cannot happen. The problem is…

‘Chilonda chatukusira mu DPP’

Bwerani poyera mulankhule kwa Amalawi. Awa ndi mawu a akadaulo pa ndale pamene alangiza mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika ndi wachiwiri wake Saulos Chilima kuti alankhulepo pa mpungwepungwe omwe wabadwa m’chipanicho. Akadaulowo, Emily Kamanga ndi Henry Chingaipe alangiza izi kutsatira kusamvana pa yemwe atengere chipanicho kuchisankho cha 2019. M’sabatayi, anthu akhala akubwera poyera ndi…

Moto buuu! 2019 yafukiza zipani

Fumbi lachita kobooo! m’zipani pamene kwangotsala chaka chimodzi kuti chisankho cha patatu chichitike m’dziko muno. Chisankho cha patatu chidzakhalako pa 21 May 2019. Izi zili choncho, zikuoneka kuti m’zipani mwabuka moto pomwe nkhondo yolimbirana wodzaimira zipanizo yakula. Pamene ena m’chipani cha DPP akhala akunena kuti Peter Mutharika apereke mpata kwa wachiwiri wake Saulos Chilima kuti…

Akufuna boma likweze malipiro

Bungwe loona za ufulu wa anthu ogwira ntchito la Malawi Congress of Trade Union (MCTU) lapempha boma kuti likweze mlingo wa ndalama zotsikitsitsa zomwe munthu angalandire, komanso kuti anthu amene amalandira ndalama zochepera K50 000 pamwezi asamakhome  msonkho. Polankhula pamwambo wokumbukira tsiku la ogwira ntchito Lolemba ku Lilongwe, mkulu wa bungwelo Luther Mambala adapempha boma…

Amalawi alankhula: Masiku 30, boma liyankhe—Gift Trapence

Malawi adayaka moto dzulo m’zigawo zonse pamene anthu adayenda pokhumudwa ndi ntchito za boma la DPP. Mfundo yamangidwa ndiyoti boma liyankhe m’masiku 30 apo ayi Amalawi abwereranso kumsewu. Mmodzi mwa amene adakonza zionetserozo, Gift Trapence wa bungwe la Centre for the Development of People (Cedep), adati ayembekezera kuti boma liwayankhepasanathe masiku 30. “Pali nkhani zambiri…

‘Mundibwezere voti yanga’, amalawi athafulira APM pazionetsero

Amalawi athera Chichewa mtsogoleri wa dziko lino komanso nduna zake pa zionetsero zomwe zidachitika Lachisau. Zionetserozo zidatsogoleredwa ndi amipingo, amabungwe komanso azipani amene amakakamiza boma kuti liyankhepo pa mavuto amene dziko lino likudutsamo. Mwa zina ndi kuuza mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika kuti athothe nduna ya zachuma Goodall Gondwe komanso ya maboma ang’ono Kondwani…