Ziphuphu m’kalembera

Pamene kalembera wa unzika za dziko lino ali mkati, zadziwika kuti anthu ena apeza mpata wosolola m’matumba mwa Amalawi omwe akutenga nawo gawo lolembetsa mukalemberayu. Amalawi ena akumafunsidwa kupereka K500 kapena kuposera apo kuti apeze mwai wa fomu yolembapo mbiri yawo. Izi zikumachitika makamaka pamalo akalemberayu pakakhala khwimbi la anthu omwe akumauzidwa kuti mafomu atha…

Agwira othandiza akunja kupeza zitupa zaunzika

Mmiyezi iwiri yokha chiyambireni kalembera wa zitupa za unzika, Amalawi ena ayamba kugwidwa akuthandiza nzika za mayiko ena kupeza zitupazi. Akuluakulu ena ati uku n’kusowa chikondi ndi dziko lawo la Malawi. Nzika zitatu za ku Mozambique zagwidwa kale m’boma la Dedza pomwe zimafuna kulembetsa m’kaundulayu pamalo olembetsera a Umbwi mothandizidwa ndi mayi wa Chimalawi. Mneneri…

Akhazikitsa tindege tothandiza zaumoyo

  Pali chiyembekezo chakuti mavuto omwe amakumana nawo ogwira ntchito m’zipatala za kumidzi ndi anthu okhala m’maderawo achepa ndi makina  a tindege otchedwa drone m’Chingerezi polumikizitsa maderawa ndi zipatala zikuluzikulu. Unduna wa Zaumoyo, nthambi yoyendetsa za maulendo a pa ndenge ndi bungwe loyang’anira za umoyo wa ana la Unicef atsimikiza za ndondomekoyi yomwe ati yayamba…

Otsutsa adzudzula MEC

Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) liyenera kutambasula bwino za pangano lake ndi bungwe limene likupereka zitupa za unzika la National Registration Bureau (NRB) pa zoti lidzagwiritsa ntchito zitupazo pa kalembera wa chisankho cha 2019, watero kadaulo pa ndale Mustafa Hussein. Zipani za ndale, makamaka zotsutsa boma zakhala zikunena kuti chikonzero cha MEC n’kufuna kudzathandiza…

Be part of solution to end child marriages—First Lady

First Lady Madame Gertrude Mutharika has challenged Malawians to be champions in protecting children especially girls who are often subjected to early and forced marriages. She was speaking at Bingu International Convention Centre (BICC) in Lilongwe during the launch of the Integrated Mass Media Campaign on Ending Child Marriages. Mutharika said the campaign dubbed Lekeni…

UN demands more action on albino attacks

The United Nations (UN) has asked Malawi to do more in the fight against attacks on persons with albinism. UN Women country representative Clara Anyangwe made the remarks yesterday during the International Albinism Awareness Day commemorations in Ntcheu. “The continued attacks on persons with albinism is an indication that there is still a lot more…

LL school commemorates Menstrual Hygiene Day

Southern Africa Aids Trust (Saat) has advised school-going girls to take pride in menstruation as a natural gift for women and not a challenge to deter them from progressing with education. Saat country director Robert Mangwazu-Phiri offered the advice recently during the commemoration of Menstrual Hygiene Day at Chiwamba primary school in Lilongwe. He observed…

Boma, kupyolera m’nthambi ya National Registration Bureau (NRB), Lachitatu lidayamba gawo loyamba lolemba Amalawi kuti akhale ndi zitupa za unzika. Gawo loyamba la kalemberayu idayamba m’maboma a Nkhotakota, Ntchisi, M   chinji, Kasungu, Salima ndi Dowa. Ntchitoyi, imene ikhale m’magawo atatu, idya K36.5 biliyoni ndipo Amalawi 9 miliyoni alowa m’kaundula. Malinga ndi mneneri wa nthambi ya…

Akukambirana zolola ana a chi Rasta m’sukulu

Unduna wa za maphunziro wati ukukambirana ndi ma Rasta komanso unduna wa za malamulo pa za ana 26 amene ma Rasta adapempha kuti aziloledwa kuphunzira m’sukulu za boma ali ndi tsitsi la mizere—madiredi. Anawa, amene padakali pano sakupita kusukulu, akuimira ana ena onse a ma Rasta amene amaletsedwa kusunga tsitsi lopotana m’sukulu za boma za…

Boma likonzekera Ebola

Unduna wa zaumoyo wasonjola komiti yoyang’anira za kapewedwe ndi kuthana ndi matenda a ebola kuti ikhale chile zitamveka kuti matendawa abuka m’dziko la Democratic Republic of Congo (DRC). Malingana ndi undunawu, kuyambira mwezi wa April, 2017, anthu 11 apezeka ndi matendawa m’dzikolo ndipo mwa  anthuwa, atatu adamwalira nawo zomwe zikupereka nkhawa kuti akhoza kusefukira m’maiko…

LL police recover 3 vehicles

Lilongwe Police anti-motor vehicle theft unit have arrested five people and recovered three vehicles which are believed to have been stolen in separate incidents of similar pattern within the city. Central Region Police spokesperson Nolliettie Chihana has confirmed the arrest of Peter Mphepo, 53; Gladson Banda, 44; Wilson Chimbalu, 44; Lingson Binton, 31; and Mishoni…

Malungo atheretu—Unduna

Pamene dziko limakumbukira ntchito yothana ndi malungo Lachiwiri, boma la Malawi lati likuyesetsa kuti malungo m’dziko muno atheretu. Bungwe la zaumoyo pa dziko lonse la World Health Organisation (WHO) lidapatula 25 April chaka chilichonse kukhala tsiku lokumbukira nthendayi, imene imatengera kuli chete anthu ambiri, makamaka amayi oyembekezera ndi ana a mu Africa.aria Ndipo pamene mutu…

More residents accessing  potable water in Chikwawa

  Water for People, a non-governmental organisation (NGO) implementing water and sanitation programmes in Senior Chief Chapananga in Chikwawa, says it is making progress in ensuring local people of the area have potable water. This was revealed recently when Minister of Health Peter Kumpalume gave Senior Chief Chapananga an Open Defaecation Free certificate at an…

Malawi, China sign pact on traditional medicine

  Experts from China will soon be coming to Malawi for technical assistance in the extraction and processing of traditional medicines which have become the Ministry of Health’s fresh focus in combating some ailments. The development follows a memorandum of understanding (MoU) Ministry of Health and the Chinese government signed at the ministry’s headquarters in…

Alandira K14 biliyoni yotukulira maphunziro

Maiko ndi mabungwe omwe amathandiza boma ati apereka thandizo la K14 biliyoni ku unduna wa zamaphunziro zotukulira maphunziro m’sukulu za pulayimale. Lonjezoli lili mumgwirizano wa pakati paboma la Malawi ndi maiko a Norway ndi Germany kudzanso banki yayikulu padziko lonse ya World Bank ndi bungwe la United Nations Children’s Fund (Unicef). Mbali ziwirizi zidasayinirana mgwirizanowu…

Kwezani ndalama ku umoyo—MHEN

Mavuto a zaumoyo m’Malawi muno ndiye ndi osayamba. Odwala kuthinana m’zipatala, mankhwala kusowa, madotolo ochepa komanso zipatala zotalikana. Mkulu wa bungwe la Malawi Health Equity Network (Mhen) George Jobe, wati mavuto onsewa akudza chifukwa dziko lino silikuyika K15 ya K100 ya ndondomeko ya zachuma ku ntchito zaumoyo. Jobe adati maiko a mu Africa kuphatikizapo Malawi…

Agro players vie for enhanced chemical technologies

Agricultural companies working as a consortium in the country have embarked on a farmer awareness campaign on the use of farming chemical technologies for bumper harvests. Farmers Organisation Limited (FOL), Pannar seed company, Funwe Seed Company, Peacock Seed Company and Agricultural Input Supplies Limited (AISL) have been running demonstration plots with farmers in some parts…

Chisankho chachibwereza chilipo pa 6 June

Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lakhazikitsa pa 6 June 2017 kuti Amalawi adzaponye voti yachibwereza kummwera cha kummawa kwa Lilongwe patangotha mwezi bwalo lamilandu la apilo litagamula kuti chisankho cha kuderali sichidayende bwino. Chigamulochi chidaperekedwa potsatira dandaulo la yemwe ankaimira chipani cha Malawi Congress Party (MCP) Ulemu Msungama kuti chinyengo chidachitika pachisankhocho.…

‘Admarc isagulitse chimanga kunja’

Bungwe la Admarc lisatengeke ndi zakuti dziko lino likhoza kukolola chimanga chochuluka chaka chino n’kugulitsa chimanga kunja padakalipano, mkulu wa mgwirizano wa mabungwe a zaulimi la CisaNet Tamani Nkhono-Mvula watero. Nkhono-Mvula adauza Tamvani pomwe Admarc ikulingalira zogulitsa chimanga chimene lidagula ku Zambia kumaiko a Kenya ndi Tanzania. Izi zadza pomwenso mtsogoleri wa dziko lino Peter…