A ku Mozambique akulembetsa  mavoti

Nzika zina za m’dziko la Mozambique  zikulembetsa nawo m’kaundula wa mavoti ku Dedza popofuna kuti zidzavote nawo pa  chisankho cha magawo atatu chomwe chilipo pa 20 May, 2014. Mneneri wa polisi ku Dedza Edward  Kabango wati panopa apolisi anjatapo kale nzika imodzi ya dzikokolo, Edward  Tenganibwino, wa zaka 28, wochokera m’mudzi mwa Golong’ozo yemwe amafuna …

Papsa tonola, kusolola kwaphweka ku Kapitolo

Kwagwa papsa tonola kulikulu la dziko lino (Capital Hill) ku Lilongwe komwe akuluakulu ena ogwira ntchito zowerengera chuma cha boma akuyendera zija amati mbuzi imadya pomwe aimangirira. Sabata yokha ino akuluakulu awiri ogwira ntchito yowerengera ndalama za boma anjatidwa atapezeka ndi ndalama zokwana K10.8 million ndi ndalama zina zakunja zokwana $25,400 (pafupifupi K10 miliyoni) zomwe…

EU tells police to resist corruption

The European Union (EU) has urged the Malawi Police Service (MPS) to avoid indulging in corrupt practices to retain public trust on matters of security and order. EU head of delegation to Malawi, Alexander Baum made the appeal yesterday during the launch of the Malawi Police Anti-Corruption Policy in Lilongwe. He said poor incentives such…

‘Samalani ndi mitengo ina’

Kadaulo achenjeza zobzala bluegum, malaina m’munda Katswiri wa zakasamalidwe ka nthaka m’boma la Lilongwe, Edson Chagunda, wati alimi akuyenera kusankha mitengo yobzala m’munda pofuna kuthana ndi mavuto a kuonongeka kwa nthaka. Polankhula mwapadera ndi Uchikumbe, Chagunda adati pali mitengo ina yomwe imaononga nthaka komanso kumwa madzi omwe mbewu zikadagwiritsa ntchito ndi kukula bwino. Iye wati…

Clinton tips Malawi on development

Former US president Bill Clinton has urged Malawians to work hard to improve the country’s capacity on self -reliance. Clinton spoke after touring Kamuzu Central Hospital (KCH) where his Clinton Development Foundation (CHF) supports the laboratory unit with equipment and medical resources. “I have always known Malawians as hard-working people. However, I would like to…

Kaundula wa mavoti akuyenda bwino

A Malawi m’madera ena adakhamukira kumalo olembetsa maina awo m’kaundula wa chisankho cha pa 20 May 2014. Malinga ndi mphunzitsi wa za ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, izi ndi chisonyezo chakuti anthu ali ndi njala yofuna kusankha atsogoleri awo, zimene zingachititse boma la PP kugwa, kapena kulamuliranso zaka zina zisanu. Chinsinga amalankhula izi…

Mayeso alembedwanso?

Unduna wa Maphunziro wati ukudikira chikalata chochokera kubungwe loona za mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) usadalengeze ngati mayeso a Malawi School Certificate of Education (MSCE) angapitirire kapena ayi. Mneneri wa undunawu Rebecca Phwitiko adanena izi kutsatira zomwe ena amapempha undunawo kuti uimitse mayesowo chifukwa adabooka ndipo ophunzira ena adagwidwa ndi malikasa mayeso  asadalowe…