Akadaulo a zandale ena ati zomwe akuchita akuluakulu a zipani polekelera kukokanakokana m’zipani zawo n’kutsekeleza mwayi wodzapambana pachisankho cha 2019. Katswiri wa za ndale kusukulu ya ukachenjede ya University of Livingstonia (Unilia) George Phiri komanso kadaulo pankhaniyi ku Chancellor College Happy Kayuni amathirira ndemanga pa kukokanakokana komwe kwayala nthenje m’zipani za Malawi Congress Party (MCP),…
Achenjeza zipani
