Tamvani - Weekend Nation
Atenga Hule
- Category: Tamvani - Weekend Nation
- Published Date
- Written by Lawrence Kadzitche
Nthawi zambiri timangomvera nyimbo zauzimu mwachibwana; timangosangalala ndi mawu kapena maimbidwe a zida ndi zing’wenyeng’wenye.
More... 1 comment
‘Afunse bwino za mathanyula’
- Category: Tamvani - Weekend Nation
- Published Date
- Written by Bobby Kabango
Amabungwe ena omwe siaboma, mafumu ndi anthu ena otumikiridwa ati pakhale kufufuza kokwanira pa zochotsa kapena kusungabe lamulo lokhudza ukwati wa mwamuna ndi mwamuna kapena mkazi ndi mkazi okhaokha.
