Chichewa

Galu kusaka mbuyake

Listen to this article

dog

Nkhani ya agogo anayi amene adaphedwa ku Neno kaamba koganiziridwa kuti adapha munthu m’matsenga idakhudza Amalawi ambiri. Zoona, ngakhale mkulu wa apolisi Lexten Kachama amene Lachitatu adapita komweko kukalangiza anthu za milandu yokhudza ufiti. Chomwe chidapatsa ena chidwi ndi galu ali apayu amene amaoneka kuti amasakasaka mbuye wake. Galuyo adalowa m’gulu la anthu nkubwerera osapeza mbuye wakeyo. Kapena naye amangofuna kumva nawo uthenga wa ufitiwo?

Related Articles

Back to top button