Category: Chichewa

Lamulo lochotsa mimba ladengula

… Akufuna ogwiriridwa, opatsana pathupi pachibale ndi ana achichepere aziloledwa kuchotsa pathupi   Lamulo lokhudza kuvomereza kuti amayi akhoza kumachotsa mimba movomerezeka latsala pang’ono…
Makuponi otsiriza afika m’zigawo

Mabanja ovutikitsitsa tsopano akhoza kumwetulira kutsatira kaamba ka kubwera kwa makuponi otsiriza a zipangizo zaulimi zotsika mtengo. Boma lati lalandira makuponi omaliza, zomwe zipangitse…
Katsoka: Mutu wa alakatuli

Ulakatuli ndi limodzi mwa maluso omwe akuphukira kumene m’dziko muno. Zaka zambiri zapitazo, anthu samatenga ndakatulo ngati njira yofalitsira uthenga kapena kuphunzitsa monga momwe…

  Kwawo sindidziwako Agogo, Ndinapeza mwamuna kudzera patsamba lino ndipo ndikuyamika chifukwa chondithandiza. Komano vuto langa ndi loti amakana kuti ndikadziwe kwawo, koma kwathu…
Zionetsero ponseponse

Nyimbo imene idavuta pa Wenela tsiku limenelo idali ya Lucius Banda, Jennifer. Mundiuzire Jennifer Ayeayeyeye Mundiuzire afatse Ayeayeyeye Kokafuna maunitsi akatengako Edzi. Abale anzanga…

Chaka chino zangokumanizana ndendende kuti lero, pa 21 November, ndi tsiku loganizira nsomba ndi ntchito za usodzi padziko la pansi (World Fisheries Day). Bungwe…
Lingalirani zobzala mitengo

  Mvula masiku ano ikugwa mwanjomba, kutentha kukuonjeza, madzi sachedwa kuuma komanso nthaka ikukokoloka modetsa nkhawa. Awa ndi ena mwa mavuto omwe akatswiri akuti…