Category: Chichewa

Akunyengana ndi mnzanga Zikomo Anatchereza, Ndakhala pabanja zaka 7 ndipo tilinso ndi mwana wa zaka 7. Tsiku lina mwanayo adathyoka mkono ndipo adatigoneka kuchipatala…
Ndithu chili ndi mwini

Kusankha Balaba Kumukana Yesu Usapange mistake, chonde chonde Nyimbo ya Evans Meleka idali kuphulika pa Wenela tsiku limenelo. Ya Ndirande iyi! Machinjiri inayo! Za…
Kudya moyenera n’kofunika

  Kudya ndi moyo koma woona za kadyedwe koyenera ku Lilongwe University of Agriculutre and Natural Resources (Luanar), Dr Alexander Kalimbira, wati munthu amayenera…
Nandolo mpatali

  Ubwino wa nandolo si uli pa kupeza ndalama zochuluka kokha komanso zina zambiri, watero mkulu woona za mbewu za m’gulu la mtundu wa…
Aganyu okhala ndi ziphaso

Mwa zina zidabweretsa mawu woti tawuni ya Limbe imalira ochenjera, ndi kuberedwa kwa katundu ndi munthu yemwe udamukhulupirira kuti akunyamulire, wa ganyu. Tsopano padepoti…
Zili bwino—PAC

Nduna yakale ya zaulimi George Chaponda yamangidwa patatha masiku 43 kuchokera pamene nthumwi kumsonkhano wa Public Affairs Committee (PAC) lidapatsa boma masiku 30 kuti…
Ziphuphu m’kalembera

Pamene kalembera wa unzika za dziko lino ali mkati, zadziwika kuti anthu ena apeza mpata wosolola m’matumba mwa Amalawi omwe akutenga nawo gawo lolembetsa…
Maliro pa chisangalalo

Mwambo wa chikondwerero choti dziko lino latha zaka 53 lili pa ufulu wodzilamurira lidasanduka chisoni pomwe ana 7 ndi bambo mmodzi adamwalira pokanganirana kulowa…
Sitalaka pa Wenela

Lidali Lachinayi usiku ndipo tidali malo aja timakonda pa Wenela kukambirana izi ndi izo. Adachuluka adali madilaivala ndi makondakitala a minibasi. Ife ojiya, osenza…

ANATCHEREZA Akundikakamira Ndili ndi mkazi yemwe ndili naye mwana mmodzi. Vuto lake ndi limodzi: amakhalira kunyoza makolo ndi abale anga. Amati banja sakulifuna koma…
Minibasi zikwera Mwachinunu

  Nthawi zonse minibasi zikamakweza mtengo, makamaka mafuta akakwera, bungwe la eni minibasi limalengeza, ndi kuika mitengo ya minibasi kuti aliyense adziwe. Koma kuchokera…
Aonjezera masiku a katemera

Mkulu wa oyang’anira zaumoyo mu unduna wa zaumoyo Dr Charles Mwansambo wati ngakhale ntchito yopereka katemera wa chikuku wa Rubella idayenda bwino, padali mavuto…