Chichewa
-
‘Kunyalanyaza kudzetsa ngozi’
Sabata yangothayi ngozi zidakuta dziko lino pomwe anthu 17 adafa. Pamene anthu amati akhazikitse mitima pansi, anthu 8 atafa pa…
Read More » -
Afufuza za mkalabongo
Zambiri zakhala zikukambidwa za mkalabongo, mowa waukali umene suchedwa kutenga amene akuumwa koma tsopano, makampani 21 akufufuzidwa pamadandaulo amene Amalawi…
Read More » -
Amalawi a nsomba ali kakasi ku Botswana
Ali mbuu, kutuwa ndi njala, Patricia Mboma ndi wokwiya ndi ganizo la boma la Botswana loletsa kuti m’dzikomo musatuluke nsomba…
Read More » -
‘Sitilembetsa mayeso’
Aphunzitsi amene alembetse mayeso a Fomu 4 a chaka chino omwe ayambe pa 22 June, aopseza kuti sadzagwira ntchitoyo ngati…
Read More » -
Atsatsidwa kugula anthu kawiri
Njonda ina yomwe ikuchita bizinesi yake ya golosale ndi chigayo pa boma ku Dowa yadandaula kuti anthu akuiwonongera mbiri chifukwa…
Read More » -
Apolisi mbweee! ku PAC
Kwa munthu wongofika kumene mumzinda wa Blantyre, ngakhale nzika za mzindawu, sabata imene yangothayi kudali chitetezo chokhwima zedi pomwe apolisi…
Read More » -
Achitira zadama mu basi
Anthu ena okhala mumzinda wa Mzuzu akhala akuchitira za dama m’mabasi omwe adaimikidwa kumsika wa Zigwagwa pafupifupi miyezi inayi yapitayi.…
Read More » -
Boma lifalitsa lipoti la zotaya mimba
Boma latulutsa lipoti la zotsatira za kafukufuku wa wokhudza za Malamulo ochotsa mimba yemwe bungwe lapadera lofufuza za malamulowo lidachita…
Read More » -
‘Ndalama zaperewera m’magawo ofunikira’
Ngakhale maunduna a zamalimidwe, umoyo ndi maphunziro alandira ndalama zochuluka kwambiri mundondomeko ya momwe boma liyendetsere chuma kuyambira pa 1…
Read More » -
Fodya wakunja wayamba kulowa
Pomwe dziko la Malawi lalima fodya wochepa ndi makilogalamu 27 miliyoni pamlingo omwe ogula fodyayu adaitanitsa, mavenda ena amachawi ayamba…
Read More » -
Chipembedzo chikukolezera kupemphapempha m’misewu
Kukhulupirira chipembedzo kukukolezera mchitidwe wopemphapempha m’misewu, zimene zachititsa kuti ntchito yochotsa opemphawa ivute, watero mkulu wa bungwe limene limachotsa ana…
Read More » -
Kalembera wa nzika wayamba
Boma, kupyolera m’nthambi ya National Registration Bureau (NRB), Lachitatu lidayamba gawo loyamba lolemba Amalawi kuti akhale ndi zitupa za unzika.…
Read More » -
Akukambirana zolola ana a chi Rasta m’sukulu
Unduna wa za maphunziro wati ukukambirana ndi ma Rasta komanso unduna wa za malamulo pa za ana 26 amene ma…
Read More » -
Boma likonzekera Ebola
Unduna wa zaumoyo wasonjola komiti yoyang’anira za kapewedwe ndi kuthana ndi matenda a ebola kuti ikhale chile zitamveka kuti matendawa…
Read More » -
Mbusa amuganizira kugwirira wozelezeka
Apolisi m’boma la Neno akusunga m’chitokosi mbusa wina wa zaka 52 yemwe amatchuka kutyi “Pastor Joshua” wa mpingo wa United…
Read More » -
Kulira, chimwemwe ndi banki m’khonde
Ngakhale adali ndi chidwi choyamba bizinezi kuti atukuke, kusowa kwa mpamba kumapondereza khumbolo. Sanderson Yuba wa m’mudzi mwa Namalima kwa…
Read More » -
Shuga apezeka posachedwa—Illovo
Mkulu wa kampani yopanga shuga ya Illovo Malawi Mark Bainbridge wati kampaniyo iyesetsa kuti shuga azipezeka chaka chonse osati kumasowa…
Read More » -
Wotokosola mnzake diso akaseweza
Khoti ya majisitireti ku Mangochi yalamula Joseph Mtambo wa zaka 25 kuti alipire K200 000 kapena akakhale kundende zaka zitatu…
Read More » -
‘Ndale pamaliro n’chitonzo’
Katswiri pa zachikhalidwe, Emily Mkamanga wati zomwe zakhala zikuchitika pa miyambo ya maliro m’dziko muno ndi belu lozindikiritsa kuti andale…
Read More » -
Malungo atheretu—Unduna
Pamene dziko limakumbukira ntchito yothana ndi malungo Lachiwiri, boma la Malawi lati likuyesetsa kuti malungo m’dziko muno atheretu. Bungwe la…
Read More »