Category: Chichewa

Sitalaka pa Wenela

Lidali Lachinayi usiku ndipo tidali malo aja timakonda pa Wenela kukambirana izi ndi izo. Adachuluka adali madilaivala ndi makondakitala a minibasi. Ife ojiya, osenza…

ANATCHEREZA Akundikakamira Ndili ndi mkazi yemwe ndili naye mwana mmodzi. Vuto lake ndi limodzi: amakhalira kunyoza makolo ndi abale anga. Amati banja sakulifuna koma…
Minibasi zikwera Mwachinunu

  Nthawi zonse minibasi zikamakweza mtengo, makamaka mafuta akakwera, bungwe la eni minibasi limalengeza, ndi kuika mitengo ya minibasi kuti aliyense adziwe. Koma kuchokera…
Aonjezera masiku a katemera

Mkulu wa oyang’anira zaumoyo mu unduna wa zaumoyo Dr Charles Mwansambo wati ngakhale ntchito yopereka katemera wa chikuku wa Rubella idayenda bwino, padali mavuto…
Otsutsa adzudzula MEC

Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) liyenera kutambasula bwino za pangano lake ndi bungwe limene likupereka zitupa za unzika la National Registration Bureau (NRB)…
Afufuza za mkalabongo

Zambiri zakhala zikukambidwa za mkalabongo, mowa waukali umene suchedwa kutenga amene akuumwa koma tsopano, makampani 21 akufufuzidwa pamadandaulo amene Amalawi amakhala nawo. M’sabatayi, bungwe…
‘Sitilembetsa mayeso’

Aphunzitsi amene alembetse mayeso a Fomu 4 a chaka chino omwe ayambe pa 22 June, aopseza kuti sadzagwira ntchitoyo ngati Unduna wa Maphunziro salandira…
Apolisi mbweee! ku PAC

Kwa munthu wongofika kumene mumzinda wa Blantyre, ngakhale nzika za mzindawu, sabata imene yangothayi kudali chitetezo chokhwima zedi pomwe apolisi adali ponseponse. Kuyambira m’mawa,…
Achitira zadama mu basi

Anthu ena okhala mumzinda wa Mzuzu akhala akuchitira za dama m’mabasi omwe adaimikidwa kumsika wa Zigwagwa pafupifupi miyezi inayi yapitayi. Mabasiwa, salinso m’manja mwa…
Fodya wakunja wayamba kulowa

Pomwe dziko la Malawi lalima fodya wochepa ndi makilogalamu 27 miliyoni pamlingo omwe ogula fodyayu adaitanitsa, mavenda ena amachawi ayamba kulowetsa fodya kuchoka m’maiko…

Boma, kupyolera m’nthambi ya National Registration Bureau (NRB), Lachitatu lidayamba gawo loyamba lolemba Amalawi kuti akhale ndi zitupa za unzika. Gawo loyamba la kalemberayu…