Chichewa
-
Luso losema ziboliboli
Luso longosema lafika apa? Basitu ntchito zake Namalenga kuti nafenso tikhale ndi popezera ndalama. Malo anu amenewa? Amenewa ndi malo…
Read More » -
TB ya kumsana imapha ziwalo
Dokotala wothandiza anthu omwe ali ndi vuto la kufa kwa ziwalo kuchipatala cha Kachere Rehabilitation Centre mumzinda wa Blantyre,…
Read More » -
Tsabola ndi waphindu, wophweka kulima
Ulimi wa tsabola umaoneka opanda pake komanso ogwetsa mphwayi, koma Benison Kuziona, mkulu wa Bungwe la Zikometso Innovation and…
Read More » -
Phindu kawawa ndi ulimi wa tsabola
Akulipirira ana awiri ku sekondale; wagula mbuzi 19 ndi nkhuku 30. Njinga, ziwiya za pakhomo komanso banja lake silikugona…
Read More » -
Gwamba wochokera kubanja loimba
M’dziko muno muli oimba osiyanasiyana. koma kukamba za oimba nyimbo zauzimu, Gwamba ndi mmodzi mwa oimba amene akusintha miyoyo ya…
Read More » -
Anatchereza
Wokondedwa Anatchereza, Zikomo chifukwa cha malangizo amene mukumapereka. Thandizeni. Ndili ndi mkazi yemwe ndakhala naye kwa nthawi ndithu. Iye adapezeka…
Read More » -
Ana avala umasiye Makolo akali moyo
Nthawi ya nkhomaliro yakwana, pamsika wa Manje mumzinda wa Blantyre ambiri akudya nsima pamene ena akusaka chakudya. Kuponya maso…
Read More » -
Ndime ya vakabu yapita, koma samalani
Ena mwa anthu okhala mumzinda wa Mzuzu ati ngakhale bwalo lounika za malamulo oyendetsera dziko lino lidati lamulo la…
Read More » -
Basi ayisempha
Tsiku limenelo sitidakhale pa Wenela. Palibe ojiya, osolola, osenza ndi oitanira amene adatsala pa Wenela. Tidakwera galimoto la mkulu wina…
Read More » -
Mameya afanana maloto
Pamene chisankhocho cha mameya atatu a m’mizinda ya dziko lino chadutsa, masomphenya a mameya onse agona polimbikitsa kuteteza malo…
Read More » -
Achenjeza zobzala chinangwa cha matenda
Katswiri oona za tizilombo toononga komanso toyambitsa matenda ku mbewu wa kunthambi ya kafukufuku ya Bvumbwe Research Station, Dr…
Read More » -
Basi ayisempha
Tsiku limenelo sitidakhale pa Wenela. Palibe ojiya, osolola, osenza ndi oitanira amene adatsala pa Wenela. Tidakwera galimoto la mkulu wina…
Read More » -
2017 yatilandira ndi zigumula
Pangotha sabata chilowereni chaka cha 2017, koma malipoti a ngozi zakudza ndi mvula m’maboma osiyanasiyana atopetsa kale. Nyumba, sukulu,…
Read More » -
Aliza abale pa Khrisimasi chifukwa cha mowa
Chaka chilichonse, 25 December ndi tsiku lachisangalalo koma chaka changopitachi lidali lachisoni m’banja la a Moses a kwa Chinthambwe…
Read More » -
Anatchezera
Ndimufunsirebe? Ndine mnyamata wa mu Lilongwe ndipo ndidagwa m’chikondi ndi msungwana wina. Ndakhala ndikuponya mawu kwa iye koma iyeyo amayankha…
Read More » -
Tikuchita bwanji ndi matewera?
Thewera loti lagwiritsidwa ntchito limaipa mmaso komanso kudetsa kukhosi. Mwina likakhala la mwana wako, komabe ambiri limativuta kuyang’ana, kuligwira…
Read More » -
Kufumuka si kulakwa, olemekezeka!
Nkhani ili mkamwamkamwa panopa ndi yoti nduna ya zaulimi, mthirira ndi chitukuko cha madzi, George Chaponda, kudzanso mkulu wa…
Read More » -
Mzungu wolemba dikishonale ya Chichewa
Dikishonale kapena kuti buku lotanthauzira mawu ndi imathandiza anthu kupeza matanthauzo a mawu omwe akuwavuta kuti amvetsetse zomwe nkhani…
Read More » -
Makuponi adza ndi misonzi
Bungwe la alimi la Farmers Union of Malawi (FUM) komanso alimi ena apempha boma kuti likonzenso ndondomeko ya…
Read More » -
Chilengedwe chibwerere ku Mwanza
Mapiri, nkhalango komanso madambo ali mbulanda. Anthu adagwetsa mitengo ndi kuotcha makala. Koma lero nkhani yasintha. Pang’onopang’ono boma la…
Read More »