Chichewa
-
Ulova wafika posauzana
Adatenga digiri ya uphunzitsi mu 2010 ku Chancellor College (Chanco), kaamba kosowa ntchito, tsopano wachoka m’tauni ndipo akukhala kumudzi komwe…
Read More » -
‘Tidagwirizira ukwati wa mnzathu’
Akuti wokaona nyanja adakaona ndi mvuu zomwe. Naye wokagwirizira ukwati wa mnzake, adakapezako banja. Izitu zikupherezera pa wolemba nkhani…
Read More » -
Akhalenso ndi moyo wautali
Tsiku limenelo ndidakwiya zedi pa Wenela. Mkwiyo wanga udali waukulu zedi moti ndidafuna kuphulika. Inde, udali mkwiyo waukulu zedi…
Read More » -
Anatchezera
Chikondi amatero? Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 20 ndipo ndili kukoleji. Ndili ndi chibwenzi chomwe tidagwirizana kuti tidzamange banja mtsogolo…
Read More » -
Richard Mbulu: Chilombo cha Mafco FC
Dzina la Richard Mbulu lasanduka nyimbo ya mizinda yonse chifukwa cha ntchito zake zomwetsa zigoli. Pano Mbulu akutsogola mu…
Read More » -
Avulaza shehe akuitanira mapemphero
Nthawi ikamathamangira 5 koloko mmawa, anthu achipembedzo cha Chisilamu amadzutsidwa kuti akachite mapemphero kumzikiti pamene shehe kapena mwazini (muezzin)…
Read More » -
Lonjezo la jb Lasanduka loto
Bambo ake adamwalira, chiyembekezo chidali pa bambo womupeza, nawonso adamukhumudwitsa pomugwiririra n’kumupatsa pathupi ndipo bwalo la milandu lidamugamula kuti…
Read More » -
Musasusukire dzombe—unduna
Ngakhale dzombe limaononga mbewu, kwa anthu ena ndi ndiwo zankhuli. Koma unduna wa zamalimidwe, ulimi wamthirira ndi chitukuko cha…
Read More » -
Kulandira mwana ndi ‘nkanulo’
Zikhulupiriro zina ukamva, mutu wake weniweni sowe. Pali zambiri zomwe makolo amakhulupilira paumoyo wa munthu kuyambira kubadwa mpaka kumwalira. Anthu…
Read More » -
Chonona chifumira kudzira
Tikamakamba za kufunika kuti pasamakhale kusiyana pa mwayi womwe amayi ndi abambo akupatsidwa, titamakumbuka za mwambi uwu wakuti chonona…
Read More » -
Agulitsa chimanga kudziko la tanzania
Pomwe boma lili pakalikiriki kuitanitsa chimanga kuchokera kunja pofuna kupulumutsa Amalawi ku galu wakuda yemwe wadutsa madera ambiri m’dziko…
Read More » -
Alimi samalani pososa
Mlimi weniweni ndiye amasamalitsa kalendala yake ya ulimi. Kuyambira mwezi watha mpaka uno, alimi amalangizidwa kuti akuyenera kuyamba kusosa. Mlangizi…
Read More » -
Akhumudwa ndi kutsika kwa nandolo
Alimi a nandolo ena m’boma la Mulanje, ati ali ndi nkhawa ndi kutsika mtengo kwa nandolo modzidzimutsa pamsika zomwe…
Read More » -
Kusamala nazale ya fodya
Pamene alimi ali pakalikiliki kusosa, alimi, makamaka a fodya ali m’malingaliro okonza nazale. STEVEN PEMBAMOYO adacheza ndi mtsogoleri wa alimi…
Read More » -
‘Akudyerera obwela’
A malawi akhala akuingidwa ngati nkhuku m’maiko ena akafuna thandizo la chipatala, koma nzika zakunja kumadzawamwera mazira zikafika m’dziko muno…
Read More » -
Alipa nkhuku 70 atatayira chimbudzi pachitsime
Gulupu Chinyamula kwa T/A Kamenyagwaza m’boma la Dedza walipitsa amayi awiri nkhuku 35 aliyense chifukwa chotaira chimbudzi pachitsime. Iye walamulanso…
Read More » -
‘Mmodzi adayenera kusiya ntchito’
Ku maintaviyu ndi komwe anthu amapezerako mwayi wa ntchito, koma kwa mtolankhani wa kanema ya Zodiak, m’chigawo cha kumpoto Angela…
Read More » -
Kusanthula ntchito ya fisi
Miyambo ya makolo ndi yambiri ndipo ina akuti siyofunika kupitirira chifukwa ikuthandizira kufalitsa kachilombo koyambitsa matenda a Edzi. Sabata yathayi,…
Read More » -
Nkhanza zapolisi zanyanya
Ophunzira 24 a kusukulu za ukachenjede apereka maina awo ku bungwe la maloya la Malawi Law Society (MLS) za nkhanza…
Read More » -
Asintha mlandu wa ‘fisi’
Apolisi Lachinayi adasintha mlandu wa Eric Aniva, amene adamangidwa ataulula kwa mtolankhani wa BBC kuti amagona ndi ana achichepere komanso…
Read More »