Chichewa
-
Lamulo la za ngozi zadzidzidzi lanunkhira
Lamulo lounika za ngozi zogwa mwadzidzidzi latsala pang’ono kupsa malingana ndi zomwe mkulu woyang’anira zopanga malamulo ku unduna wa za…
Read More » -
Chithandizo chikhalapo?
Akadaulo osiyanasiyana ati boma likambirane ndi maiko omwe amathandiza dziko lino pa kusemphana kwawo pa nkhani yokhudza mkulu wabungwe lolimbana…
Read More » -
Athana naye Chizuma
Mkulu wa bungwe lolimbana ndi katangale ndi ziphuphu a Martha Chizuma akadali ndi ulendo wautali woteteza ntchito yawo yothana ndi…
Read More » -
Mavuto okhaokha m’ndondomeko ya AIP
Mavuto amanga nthenje m’pulogalamu ya zipangizo zaulimi zotsika mtengo ya AIP ngakhale kuti nduna ya zaulimi a Sam Kawale adalonjeza…
Read More » -
Fetereza wachinyengo wafika pamsika
Pomwe mdima pa za pulogalamu ya zipangizo zotsika mtengo ya Affordable Inputs Programme (AIP) ukubalalika, tsopano palowa nkhungu ya fetereza…
Read More » -
Kunali ku ‘night of prayer’
Mc Mooly Makuni Gondwe yemwe amagwira ntchito kundende ya dziko lino ndi mkazi wake Angela Chikho yemwe ndi msilikari anakulira…
Read More » -
Amayi oyendayenda akanizana migodi
Amayi oyendayenda sakumwera madzi chitsime chimodzi m’boma la Ntchisi polimbirana migodi. Nkhaniyi ikuti pali gulu la amayi achichepere ogulitsa matupi…
Read More » -
Wa zaka 19 apha mkazi wake wa zaka 16
Nkhanza za m’banja zikuchuluka m’dziko muno moti kalembera wa 2015 adawonetsa kuti mwa amayi 100 alionse omwe adakwatiwapo 42 adachitiridwako…
Read More » -
Aphungu akumana
Mkumano wa aphungu aku Nyumba ya Malamulo ulimkati ku Lilongwe ndipo mtsogoleri wanyumbayo a Richard Chimwendo Banda ati nkhawa zikuluzikulu…
Read More » -
Akhapana kaamba ka ufumu ku ntchisi
Anthu atatu akhapidwa mpaka kugonekedwa m’chipatala pa mkangano wa ufumu wa nyakwawa Kandanda kwa Senior Chief Kalumo m’boma la Ntchisi.…
Read More » -
Ena apeza golide pa vuto la mafuta
Pomwe Amalawi akulira ndi vuto la kusowa kwa mafuta a galimoto lomwe laimitsa ntchito zambiri makamaka zodalira mafutawo, anthu ena…
Read More » -
Chiyembekezo cha amalawi ku nyumba ya malamulo
Pomwe aphungu a ku Nyumba ya Malamulo akuyamba mkumano wawo wounika bajeti ya 2022-2023 pa 14 November 2022, Amalawi ati…
Read More » -
Kauniuni wa AIP watentha
Makomiti a Nyumba ya Malamulo omwe akuunika momwe feteleza wa AIP adagulidwira kuti ndalama zina zokwana K750 miliyoni zisokonekere aluma…
Read More » -
A chakwera sakugawa maswiti
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera achenjeza nduna zawo kuti yense osatha ntchito yake achotsedwa paudindo wake chifukwa nduna…
Read More » -
Mwana apha bambo ake
Apolisi m’boma la Lilongwe, akusaka mnyamata wa zaka 17 pomuganizira kuti anamenya ndi kupha bambo ake a zaka 33 chifukwa…
Read More » -
Phindu lochuluka mu feteleza wa mkodzo
Ndi K12 000 yokha amagula feteleza wa mkodzo wokwana malita 20 ndi kusungunula n’kuthira m’munda. Akatero mlimiyo a Winston Devie…
Read More » -
Zaka 10 kwa bambo wofuna kugwiririra
Bwalo la milandu la majisitileti ku Kasungu Lachitatu lidagamula bambo wa zaka 26, a Geoffrey Kwenda kuti akaseweze kundende zaka…
Read More » -
Tipinduranji ku UNGA?
Mitima ya Amalawi ili dyokodyoko kudikira zomwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera abweretse pochoka kumsonkhano wa atsogoleri a…
Read More » -
Achenjeza boma zoimitsa Admarc
Bungwe la ogula katundu la Consumers Association of Malawi (Cama) lati boma lalakwitsa kuimitsa ntchito za kampani yake ya Admarc…
Read More » -
Zipani zina sizikukhutira ndi madera a aphungu atsopano
Zipani zina za ndale m’dziko muno zati sizikukhutira ndi momwe malire atsopano a madera a aphungu ponena kuti maganizo awo…
Read More »