Chichewa
-
Kudzula: Mpeni wofunikira kwa butchala
Popha mbuzi kapena ng’ombe amagwiritsa ntchito zida zosiyanasiyana monga nkhwangwa, zikwanje ndi mipeni. Umodzi mwa mipeniyi umatchedwa ‘kudzula’ ndipo eni…
Read More » -
Zaka 30 zolimbana ndi umphawi zapita m’madzi
Bungwe loona za maphunziro, sayansi ndi chikhalidwe mumgwirizano wa maiko a dziko lapansi la UNESCO lati dziko la Malawi lalephera…
Read More » -
Othawa nkhondo ku Mozambique asamukira ku Neno
Bungwe lothandiza anthu othawa kwawo pazifukwa zosiyanasiyana la UNCHR layamba kusamutsa anthu othawa nkhondo ku Mozambique kupita ku Luwani m’boma…
Read More » -
Khama Khwiliro: Katakwe pa nyimbo zauzimu
Khama Khwiliro ndi mmodzi mwa oimba nyimbo zauzimu amene ambiri otsata nyimbozi amamudziwa. CHIMWEMWE SEFASI adakumana naye ndipo adacheza motere:…
Read More » -
Woganiziridwa kutsatsa mafupa a munthu agwidwa
Bambo wa zaka 25, James Kanjira, ali m’chitolokosi pomuganizira kuti amachita bizinesi yogulitsa mafupa a munthu m’boma la Nkhotakota.…
Read More » -
Za kulephereka kwa zisankho
Muzina Edi mwana Edi sebe santu Muzina zizata mfana Ya muzina Sindikudziwa ngati Papa Wemba nyimboyo adaimverapo koma ndimo ndinkayimvera…
Read More » -
Anatchezera
Nditani Anatchereza? Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 20 ndipo ndili ku koleji. Ndili ndi chibwenzi chomwe tidagwirizana kuti tidzamange banja…
Read More » -
Blantyre yawala, iwalirabe
Kuyenda usiku tsopano sikukhalanso koopsa ganizo la khonsolo ya mzinda wa Blantyre lipherezeke. Mneneri wa khonsoloyi, Anthony Kasunda, wati khonsolooyi…
Read More » -
Uve wanyanya m’misika
Akugwiritsa madzi a m’zithamphwi Tituluka mumsika muno—mabutchala Kafukufuku yemwe Tamvani wachita sabata ino waonetsa kuti uve wanyanya m’misika yambiri m’dziko…
Read More » -
Likwata: Amuna aimba ng’oma, amayi navina
Likwata ndi mmodzi mwa magule amene amavinidwa pakati pa Ayao. BOBBY KABANGO adali m’boma la Chiradzulu m’mudzi mwa Njeremba kwa…
Read More » -
Mutharika achenjeza akamberembere
Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika wasonyeza kuti amatsatira ukamberembere omwe umachitika mkatikati mwa malonda a fodya ndipo wachenjeza ogulitsa…
Read More » -
Alubino akufuna chilungamo
Bambo wachialubino ku Ntcheu wati akufuna chilungamo pankhani yake yomwe akuloza chala mkulu wina wabisinesi kuti adamutsekera m’golosale ndi kumubera…
Read More » -
Pulofeti Meja wagawa dziko pawiri
Mudamvapo inu zakuti ambiri amadana ndi mneneri kwawo komwe. Izi zikupherezera masiku omaliza ngati ano. Abale anzanga, zidaliko pa Wenela…
Read More » -
Leo Mpulula: Alibe 2 koloko
Akulu, ligi ikuyamba, inu ngati kochi wa Max Bullets mwakonzeka bwanji? Tapimana ndi matimu ambiri, zikuonetsa kuti anyamata agwira ntchito…
Read More » -
Anatchezera
Ndimamukonda Agogo, Ndinali pachibwenzi ndi mkazi wina ndipo zaka ziwiri zatha pomwe tinasiyana. Pano ali ndi mwana yemwe wabereka mwezi…
Read More » -
‘Tidakhulupirirana tsiku loyamba’
Chikondi chidayambira kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College komwe Dennis Lupenga akuti atakumana ndi Sheila Chimphamba m’chaka cha 2013…
Read More » -
Aphangirana ufa
Mwambo wa mapemphero Achisilamu otchedwa dawa udasokonekera kwa Chitulu kwa T/A Mwambo m’boma la Zomba Loweruka pa 2 April…
Read More » -
Osolola ndalama za Edzi mitima ili phaphapha!
Unduna wa zaumoyo wati zotsatira zakafukufuku wokhudza kusokonekera kwa ndalama zothandizira kulimbana ndi matenda a Edzi zatuluka, koma undunawu…
Read More » -
Chenjezo: Makolo a ana opemphetsa azinjatidwa
Apolisi mumzinda wa Blantyre ati nthawi yatha ndipo tsopano ayamba kumanga makolo a ana amene apezeke akuyendayenda n’kumapemphetsa m’misewu ya…
Read More » -
Awiri afa ndi bibida ku KK
Abambo awiri amwalira ndi mowa wa kachaso m’njira zofanana koma malo osiyana m’boma la Nkhotakota. Mneneri wa polisi m’bomali, Williams…
Read More »