Chichewa
-
Alimbana ndi ntchemberezandonda ku Zomba
Unduna wa zamalimidwe wati ntchemberezandonda zomwe zabuka m’boma la Zomba zisatayitse anthu mtima chifukwa akatswiri apita kale m’madera omwe akhudzidwa…
Read More » -
Alosera mvula kugwa mochuluka
Nthambi yoona za nyengo ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati mvula yamphamvu ikhala ikugwa kwa…
Read More » -
Chaka ndi miyezi inayi ali m’chipatala osaimirira
Maloto a Alineti Molosi wa zaka 15 odzakhala namwino akhoza kufera m’mazira ngati madotolo sakwanitsa kumuchiza nthenda yozizira miyendo…
Read More » -
Anatchezera
Sitinakumanepo Anatchereza, Ndili ndi mkazi amene ndidamufunsira pafoni koma sitinaonanepo. Timangoimbirana foni basi koma amandiuza kuti amandikonda kwambiri. Ndimukhululupirire? …
Read More » -
Za maukwati, mabanja
Money is gooooood Musayense njerego, awa ndi mawu ochokera munyimbo ya Miracle Money ya mnyamata wodziwa kuimba nyimbo zauzimu, Onesmus.…
Read More » -
Zaka zinayi kwa ofuna kuba alubino
Njonda ziwiri zochokera m’boma la Mzimba Lachitatu zidagamulidwa kukasewenza jere kwa zaka zinayi ndi kugwira ntchito yakalavula gaga chifukwa chofuna…
Read More » -
Katsoka: Mtsogoleri wa alakatuli
Ulakatuli ndi limodzi mwa maluso omwe akuphukira kumene m’dziko muno. Zaka zambiri zapitazo, anthu samatenga ndakatulo ngati njira yofalitsira…
Read More » -
Adzikonzera ‘mpumulo wa bata’
Ukayenda umaona agalu a michombo ndithu. Ku Rumphi aliko oyenda masanasana pamene bambo wina wa zaka 62 wakumbiratu manda…
Read More » -
‘Mwayi kuthima kwa magetsi’
Pomwe ena akudandaula za kuthimathima kwa magetsi, ena akusimba lokoma kuti adapatirapo mwayi wabanja. Victor Mpunga yemwe pa 28…
Read More » -
Mapemphero a mvula aliko lero
Pamene ng’amba yadzetsa chikaiko choti Amalawi akhoza kukolola zochepa chaka chino, mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika lero akhala nawo…
Read More » -
Njovu ipha mlenje
Tsoka sasimba. Akanadziwa mlenje sakadapita kunkhalango ya Liwonde kukasaka nyama mozemba masiku apitawo. Patrick Maya, wa zaka 52, ndipo amachokera…
Read More » -
Si zonyengerera mu 2016—Mkulu wa polisi
Anthu ali kalikiriki kukonza mapulani a chaka chatsopano cha 2016 koma ngati mapulani ake akukhudza umbanda ndi ziphuphu, dziko lake…
Read More » -
Adakumana bwanji m’chakacho?
Ankadzapepesa maliro a mkazi wanga’ Ukwati ndi chinthu chabwino, ndipo Mulungu amasangalala nacho. Chaka cha 2015 Mulungu adadalitsa ena ndi…
Read More » -
A Malawi adalimba nazo chaka chatha
Ululu, kulavulagaga ndi kupala moto kudalipo mchaka chomwe changothachi monga momwe akadaulo mnthambi zosiyanasiyana akunenera kuti padalibe popumira koma kubanika…
Read More » -
Mudalinji m’chakachi?
Ma alubino aona zakuda Mpotopola ku Joni, Amalawi 3 200 athothedwa Anthu 106 afa ndi madzi osefukira Tili m’chaka…
Read More » -
Tidacheza nawo bwanji?
M’chaka cha 2015 tamva zikhulupiriro, miyambo komanso mbiri zosiyanasiyana za maderanso osiyana. Lero BOBBY KABANGO akutibweretsera macheza ochepa amene nkhani…
Read More » -
Kupewa nsabwe za m’fodya ndi pano
Nsabwe za mufodya ndi gwero limodzi lomwe limachititsa kuti fodya avute malonda kumsika ndipo vutoli likagwera mlimi, chaka chimenecho amalirira…
Read More » -
Mmera watuluka koma samalani, atero katswiri
Mmera watuluka ndipo momwe zikuonekera alimi ambiri akhoza kuchita mphumi chaka chino zinthu zikapanda kusintha, makamaka pakagwedwe ka mvula. Koma…
Read More » -
Abambo odzikhweza akuchuluka
Kafukufuku wa apolisi m’dziko muno waonetsa kuti abambo 90 ndiwo amadzipha pa anthu 100 alionse amene amatenga miyoyo yawo…
Read More » -
Kalonga: Waluso lothetsa makhalu
Kunja kuno oimba ndiye mbwee koma luso lawo limakhala losiyanasiyana. Ena ali ndi mawu anthetemya, ena amaimba zipangiso monga zing’wenyeng’wenye,…
Read More »