Chichewa
-
Tsogolo la fizi silikudziwika
Zenizeni pankhani yoti fizi yokwera m’sukulu za sekondale ndi sukulu za ukachechenjede za boma ipitilire kapena ayi zidziwika posachedwapa…
Read More » -
Alandira upangiri pa malonda a mbewu
Ochita bizinesi yogulitsa mbewu a m’maboma 7 m’dziko muno alandira upangiri wa momwe angapewere kuononga bizinesi yawo popezeka ndi…
Read More » -
Zasokonekera ku kapitolo
Zili kukapitolo ku Lilongwe si ndizo. Pomwe apolisi achilimika kugwira ndi kutsekera galimoto zopezeka ndi milandu, oyendetsa minibasi agangalama…
Read More » -
Anatchezera
Anatchereza Ndikumanyozedwa Anatchereza, Zikomo chifukwa cha malangizo amene mukumapereka. Ine ndili pabanja ndipo pano tikutha miyezi 7 ndipo timakondana kwambiri.…
Read More » -
The Rain: Mnyamata wanthetemya
Anthu ambiri otchuka makamaka amasewero, oyimba ndi azisudzo amakonda kudzitcha maina otchukira kusiya awo a pamchombo. Mchitidwewu sudayambire kuno…
Read More » -
Zungulizunguli mu Lilongwe
Abale anzanga, inetu ukwati, nkhani ya ukwati, sindikamba nawo. Nkhani imeneyi, kwa ine ndimangoionera apo!!! Chifukwa chake nachi: Pali ana…
Read More » -
Ngozi zanyanya chaka chino—Apolisi
Apolisi ati ngozi za pamsewu m’dziko muno zachuluka ndi 18 pa ngozi 100 zilizonse poyerekeza ndi chaka chatha nyengo…
Read More » -
Mabungwe athotha galu wakuda ku MJ
Anthu m’boma la Mulanje omwe adakhudzidwa ndi njala kaamba ka ngozi za kusefukira kwa madzi komanso chilala kumayambiriro a…
Read More » -
Boma likonzekera el nino—chilima
Boma lati alimi ndi anthu m’dziko muno asanjenjemere ndi lipoti la nthambi ya zanyengo loti chaka chino kukhoza kukhala…
Read More » -
Ku Machinga akonzekera ulimi wa fodya
Alimi a m’makalabu 7 ati chaka chino akonzeka kulima fodya wochuluka ncholinga chosintha mabanja awo pachuma popeza iwo amakhulupirira…
Read More » -
Bwanji nkhuku yoweta sagula pamsika?
Achewa ali ndi njira zosiyanasiyana zoperekera malango pakati pawo. Njira zina ndi monga nthano, magule, ndakatulo, chinamwali ndi miyambi ndi…
Read More » -
Msika wa zondeni ngosayamba
Katswiri wa zamadyedwe m’dziko muno, Chrispine Jedegwa, akupanga ndi kugulitsa ufa wa mbatata ya kholowa yamakolo yotchedwa zondeni yomwe…
Read More » -
Bzalani mbewu zocha msanga—Lipita
Woyendetsa ntchito za ulangizi ndi njira zamakono za ulimi muunduna wa zamalimidwe, Wilfred Lipita, wati alimi akuyenera kutengerapo phunziro…
Read More » -
Atukuka ndi kukwatitsa mitengo ya zipatso
Masiku ano nkhani ili mkamwamkamwa paulimi ndi yogwiritsa ntchito mitundu ya mbewu zamakono zomwe akatswiri adayesa n’kupeza kuti zili…
Read More » -
Khrisimasi ya maluzi
Kwangotsala masiku anayi kuti chisangalalo cha Khrisimasi chifike pachimake koma ochita bizinesi zosiyanasiyana akudandaula kuti sizikudziwika kuti nyengoyi yafikadi…
Read More » -
‘Ndimafuna mwamuna wadzitho’
Felix Mwamaso ndi mmodzi mwa akatswiri osewera nkhonya mdziko muno. Koma kuti zonse zizimuyendera tayale choncho pali nthiti yake,…
Read More » -
Minibasi zivuta pa Wenela
Si kuti ndikamba za kutentha kwa pa Wenela. Si kuti ndinena za kukwera mtengo kwa zinthu. Si kuti ndinena…
Read More » -
Pewani chipalamba posamala mitengo
Kampani yogula fodya ya Limbe Leaf Tobacco Company yati makolo azitsogolera ana pantchito yobzala mitengo kuti m’dziko muno…
Read More » -
Boma liganizire bwino pa sabuside
Adzavutika: Nkhalamba ndi ana amasiye Mkonzi, Ndalemba kalatayi kutsatira zomwe nduna yoona zaulimi a Allan Chiyembekeza adanena masiku apitawa. Mukunena…
Read More » -
Akufuna mayankho pa njala ya m’zipatala
Mabungwe omwe si aboma ku Rumphi ati akudikirabe yankho kuchokera kwa mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika pa zakusowa…
Read More »