Chichewa
-
Makuponi otsiriza afika m’zigawo
Mabanja ovutikitsitsa tsopano akhoza kumwetulira kutsatira kaamba ka kubwera kwa makuponi otsiriza a zipangizo zaulimi zotsika mtengo. Boma lati lalandira…
Read More » -
‘Kupitakufa? Mbiri yakale imeneyo!’
Matenda a HIV/Edzi asokoneza miyambo ina monga mwambo wa kupitakufa, womwe umapereka mphamvu kwa ‘fisi’ kuti akakonze maliro pocheza ndi…
Read More » -
Katsoka: Mutu wa alakatuli
Ulakatuli ndi limodzi mwa maluso omwe akuphukira kumene m’dziko muno. Zaka zambiri zapitazo, anthu samatenga ndakatulo ngati njira yofalitsira uthenga…
Read More » -
Anatchezera
Kwawo sindidziwako Agogo, Ndinapeza mwamuna kudzera patsamba lino ndipo ndikuyamika chifukwa chondithandiza. Komano vuto langa ndi loti amakana kuti…
Read More » -
‘Tinkakalongosola za ntchito’
Okaona nyanja amakawonadi ndi mvuu zomwe. Mawuwa apherezedwa ndi ukwati wa Amos Mazinga wa ku Dowa m’mudzi mwa Ngozi…
Read More » -
Ophunzira asanu anjatidwa ku Nkhotakota
Apolisi Lolemba adamanga ophunzira asanu a sukulu ziwiri za m’boma la Nkhotakota ndi kuwatsegulira mlandu wofuna kudzetsa chisokonezo. Mneneri…
Read More » -
Chilango chowawa kwa wogulitsa nyama ya galu
Bwalo la majisitireti la Balaka lapereka chilango chowawitsa kwa mkulu amene wakhala akugulitsa nyama yagalu kwa zaka 14. Pamene…
Read More » -
Zionetsero ponseponse
Nyimbo imene idavuta pa Wenela tsiku limenelo idali ya Lucius Banda, Jennifer. Mundiuzire Jennifer Ayeayeyeye Mundiuzire afatse Ayeayeyeye Kokafuna maunitsi…
Read More » -
Msika wa fodya wa okushoni ukuponderezedwa
Kampani yoyendetsa malonda a fodya pamsika wa okoshoni ya AHL Group yauza alimi kuti akhale tcheru pogulitsa fodya wawo…
Read More » -
Vuto la madzi lakula ku Mulanje
Anthu a m’dera la mfumu Mpweshe komanso Khunyeliwa m’dera la T/A Juma m’boma la Mulanje akuvutika kuti apeze madzi aukhondo…
Read More » -
Luanar ikhazikitsa magulu a alimi akafukufuku
Nthambi ya zaulangizi pasukulu yaukachenjede ya Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar) sabata zapitazo idakhazikitsa magulu a…
Read More » -
Nthula: Abambo ofooka kuchipinda achangamuke
Akuti abambo ena amafooka pamene akucheza ndi akazi awo chifukwa cha zina zomwe zimasowekera pamene machezawa ali mkati. Ichi nchifukwa…
Read More » -
Aphungu adzuma ndi kagawidwe ka makuponi
Ganizo la boma loyamba kugawa makuponi ogulira zipangizo za ulimi zotsika mtengo mupologalamu ya sabuside lalandilidwa ndi maganizo osiyanasiyana pakati…
Read More » -
Tsiku lokumbukira usodzi
Chaka chino zangokumanizana ndendende kuti lero, pa 21 November, ndi tsiku loganizira nsomba ndi ntchito za usodzi padziko la pansi…
Read More » -
Lingalirani zobzala mitengo
Mvula masiku ano ikugwa mwanjomba, kutentha kukuonjeza, madzi sachedwa kuuma komanso nthaka ikukokoloka modetsa nkhawa. Awa ndi ena mwa…
Read More » -
Kusintha kwa nyengo kwasokoneza ulimi wa khofi
Pamene mlimi aliyense akudandaula ndi kusintha kwa nyengo, nawo alimi a khofi sadasiidwe pamene zadziwika kuti dziko lino likukolola khofi…
Read More » -
Osabweza ngongole ya Mardef ali m’madzi
Anthu amene sadabweze ngongole ya Malawi Enterprise Development Fund (Mardef) ali m’madzi pamene ayamba kuona zakuda. Ngongole ya Mardef…
Read More » -
Mbali ina ya mnzinda wa Blantyre
Kunena zoona, mzinda wa Blantyre ukusintha. Kuona momwe mzindawu akuukongoletsera, ukhoza kuyamika. Maluwa akubzalidwa ponseponse, misewu ndi misika ikukhala yosesedwa…
Read More » -
Afa atamwa bibida wosadyera
Mneneri wa polisi ya Nkhotakota Williams Kaponda watsimikiza kuti bambo wina kumeneko wakabzala chinangwa atapapira mowa osadyera. Kaponda adati…
Read More » -
Zochitika m’minibasi
Tsikulo pa Wenela padalibe zomvera nyimbo. Nanga abale anzanga, anthu akuluakulu ngati ife tingamamvere nyimbo monga Tsika Msungwana Tsika? Nanga…
Read More »