Chichewa
-
Zochitika m’minibasi
Tsikulo pa Wenela padalibe zomvera nyimbo. Nanga abale anzanga, anthu akuluakulu ngati ife tingamamvere nyimbo monga Tsika Msungwana Tsika? Nanga…
Read More » -
Lambani wadza ndi Knock Out
Dzina la Limbani Banda, yemwe masiku ano amadzitcha kuti Lambanie Dube si lachilendo kwa otsata zoimba ku Malawi. Iye adatchuka…
Read More » -
Anatchezera
Mayi anga amandilodza Anatche, Zikomo gogo chifukwa cha malangizo amene mumapereka kwa ife awerengi anu. Anga ndi mantha pa zomwe…
Read More » -
‘Ankadzapepesa maliro a mkazi wanga’
Imfa ya mkazi kapena mwamuna wako si mathero amoyo. Mulungu amakoza njira ina kuti akupepese bwinobwino ndipo uyiwale zakale.…
Read More » -
Sabuside yayamba ndi njengunje
Pulogalamu ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya sabuside ya chaka chino yayamba koma zokhoma zilipo zambiri kuyerekeza ndi…
Read More » -
Kunalibe kubera mu 2015—Maneb
Wapampando wa bungwe loona za mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) John Saka wati bungweli ndi lokondwa kuti…
Read More » -
Alimi konzekani kukolola madzi
Mvula ya masiku ano ndi yanjomba. Zikatere mlimi amayenera kuchenjera kuti aphulepo kanthu ngakhale mvula itadula msanga. Ichi nchifukwa chake…
Read More » -
Kusamala anapiye a mikolongwe
Amati nkhuku ndi dzira, kusonyeza kuti ngati susamala dzira ndiye kuti udzalandira nkhuku za matenda zomwe sizichedwa kufa. Komanso kupanda…
Read More » -
Mphwiyo, Kasambara akadali m’chitokosi
Pamene bwalo la milandu ku Lilongwe likupitiriza kumva nkhani za amene akuwaganizira kuti adatengapo gawo posolola ndalama za…
Read More » -
Pac ifuna mayankho pa za kukwera kwa mitengo
Kukwera kwa zinthu m’dziko muno kwaika Amalawi pamoto wa mavuto zomwe zachititsa kuti bungwe la Public Affairs Committee (PAC)…
Read More » -
Gulani mbewu kwa ogulitsa ovomerezeka—Unduna
Unduna wa malimidwe walangiza alimi kuti ayenera kugula mbewu kuchokera kwa ogulitsa ovomerezeka okha poopa kugulitsidwa mbewu zoonongeka. Mlembi…
Read More » -
Dansi ndi Platinum Selector
Kuphunzira ndi chinthu chokoma ndipo ukasakaniza ndi luso lina la manja kukomako kumankira patali. Achinyamata ambiri omwe akuchita bwino…
Read More » -
Chikondi chiphetsa amuna awiri
Nthawi zina chikondi chikafikapo, chimazunguza mutu. Amuna awiri m’maboma a Machinga ndi Zomba adzikhweza sabata yathayi nkhani ya chikondi…
Read More » -
Apatsidwa upangiri wa chitukuko
Anthu okhala kumudzi ali ndi mphamvu komanso ufulu woitanitsa chitukuko cha mtundu wina uliwonse kudera lawo kotero kuti kudzipereka pantchitoyo…
Read More » -
Zitukuko pa Wenela
Nyengo yasintha abale anzanga. Chikuchitika nchiyani? Pano pa Wenela, usiku winawo kudatentha zedi moti usiku onse ndimangokhalira kudzikanda. Kutembenuka…
Read More » -
anatchezera
Akunyengana ndi mnzanga Zikomo Anatchereza, Ndakhala pabanja zaka 7 ndipo tilinso ndi mwana wa zaka 7. Tsiku lina mwanayo…
Read More » -
‘Tinkaimba limodzi kwaya’
Mdalitso suoneka pakudza munthu umangozindikira walandira mphatso koma osadziwa kuti yachoka kuti malingana ndi ntchito zomwe ukuchita monga momwe…
Read More » -
Asimbe lokoma ndani?: Civo, Manoma aswana mu Standard Bank
Pali ntchito mawa pabwalo la Civo mumzinda wa Lilongwe pamene timu ya Civo United ichapane ndi Mighty Be Forward…
Read More » -
Mafumu ‘okwatitsa’ ana athothedwa
Kachindamoto achotsa mafumu anayi Ana 549 abwerera kusukulu ku Dedza Kampeni yothamangitsa ana kubanja kuti abwerere kusukulu yafika pagwiritse m’boma…
Read More » -
Malamulo a ukwati akutsutsana
Kutanthauzira lamulo lokhudza maukwati a ana kukhala kovuta tsopano pamene pali kusemphana pakati pa zomwe zidalembedwa m’malamulo oyendetsera adziko lino…
Read More »