Chichewa
-
Agumula chiliza nkutengamo alubino
Adaikidwa m’manda pa 27 May m’chaka cha 2000. Koma zodabwitsa zachitika pa 17 October 2015 pamene anthu olusa agumula…
Read More » -
Mwambo wa maliro wasintha ku CoM
Sukulu ya zaudotolo ya College of Medicine (COM) yasintha momwe mwambo wa maliro panyumba ya chisoni ya pasukuluyo mumzinda…
Read More » -
Anatchezera
Akumandiipitsa Zikomo agogo, Ndili ndi chibwenzi ndipo makolo akudziwa ngakhale kuti ndi mwamphekesera chabe. Nthawi ina bambo ake (osati omubereka)…
Read More » -
Mpira uthera panjira wosewera atamwalira
Anthu akugwedeza mitu yopanda nyanga ku Choma, m’boma la Mzimba kaamba ka imfa ya mnyamata wa Fomu 3 pasukulu…
Read More » -
Kuchitsedwa ntchito ndi zina
Mourinhao ndi mmodzi mwa anzanga amene ndimacheza nawo pa Wenela. Sindikudziwa kuti nchifukwa chiyani mkuluyu amakonda Arsenal. Momwe amaonekera, nzeru…
Read More » -
Kasambara: Kulimbikitsa anthu mkuimba
Martha Kasambara ndi woimba nyimbo za uzimu wokhala ku Mzuzu. Iye ali ndi zimbale ziwiri ndipo mu December chaka chino…
Read More » -
‘Idali nyengo ya pasaka’
Wina adapitira ntchito yokatola zochitika pa tchuthi chokumbukira mazunzo ndi kuuka kwa Ambuye Yesu pomwe wina adapita kukapuma monga…
Read More » -
Kalikiliki popewa ngozi za madzi
Pamene nkhani yolosera mvula ili mkamwamkamwa, boma lati lili pakalikiliki kuti madzi osefukira amene amasautsa m’madera ena chaka chino lisakhale…
Read More » -
Kulira kwanyanya m’zipatala
Kubangula ndi kulira mokweza kukumveka m’zipatala za m’dziko muno pomwe boma lachepetsa ndalama zopita kuntchito za chipatala potsatira mavuto a…
Read More » -
Moto lawilawi mu TNM Super League
Ligi ya TNM yafika pa lekaleka pamene matimu ena akutenga mapointi ndipo ena kutaya mwachibwana pamene ligiyi tsopano yalowa sabata…
Read More » -
Eid al Adha: Chikondwerero chopereka nsembe
Chaka ndi chaka a chipembedzo cha Chisilamu amakhala akuzinga ziweto nthawi ina. Pa mwambowu, Asilamu amakhala akutsatira zomwe Mulungu adalamula…
Read More » -
Osataya za makolo
Kulosera nyengo nkotheka Pamene zikuoneka kuti ngozi zina zadzidzidzi zimene zakhala zikuchitika kaamba kolephera kulosera kubwera kwa ngozi zotere,…
Read More » -
Anatchezera
Ndimamukonda Agogo, Ndinali pachibwenzi ndi mkazi wina ndipo zaka ziwiri zatha pomwe tinasiyana. Pano ali ndi mwana yemwe wabereka mwezi…
Read More » -
‘Kudali ku mapemphero a Scom’
Patha zaka zisanu tsopano Dyson Milanzie yemwe ndi mkonzi wa mapologalamu kuwailesi ya kanema ku MBC-TV ali pabanja ndi njole…
Read More » -
Ng’anga yochotsetsa mimba ithawa ku Mchinji
Kwa Brenda Tadi, sing’anga Nasikiti udali ulalo wochotsera pathupi kufuna kuzemba uchembere omwe tate wake sakudziwika koma mapeto ake watsikira…
Read More » -
Wa zaka 18 akaseweza zaka 18
Bwalo lamilandu mumzinda wa Mzuzu lagamula Mulolo Nkhata wa zaka 18 kukakhala kundende zaka 18 atamupeza wolakwa pamlandu wogonana ndi…
Read More » -
Lipy G: Woimba za chinyamata
Masiku ano kwadza oimba achinyamata amene akumaimba nyimbo zawo zothamanga kwambiri. Kulitu anyamata monga Nepman, Blasto, Piksy ndi ena otero…
Read More » -
Kulimbana ndi alaliki
Ndidakhala pa Wenela tsikulo kubwira mpweya, uku ndikuitanira basi. “Ndirande iyi! Machinjiri iyo! Ntcheu-Balaka cha uko!!!” ndidali kutero. Pajatu masiku…
Read More » -
Wezzie: Chiphadzuwa chonenepa cha Mzuni
Sukulu yaukachenjede ya Mzuzu University idasankha chiphadzuwa chonenepa Loweruka sabata yatha pomwe adali ndi chisangalalo chawo cha Social Weekend. Mtolankani…
Read More » -
Anatchezera
Sabata zingapo zapitazi, takhala tikulengeza kuti patsamba lino tizikupatsirani Anatchereza ndi malangizo pamavuto amene mumakumana nawo. Mavutowa akhoza kukhala a…
Read More »