Chichewa
-
Asaka ofukula manda ndi kutengamo ziwalo
Apolisi ku Kanengo mumzinda wa Lilongwe ati akufunafuna anthu aupandu omwe adafukula manda ndi kudula ziwalo za mtembo wa…
Read More » -
Atudzula ziwalo za mwamuna wake
Pamene nkhanza zambiri zomwe zimachita zimakhakla zochokera kwa abambo kupita kwa amayi, Loveness Nakayuni wa m’mudzi mwa Chapyoka, T/A Mwaulambia…
Read More » -
Lutepo wakundende
Bwalo lalikulu la milandu ku Zomba (High Court) Lachisanu lapitali lalamula Auswald Lutepo, yemwe ndi mmodzi mwa anthu omwe akuyankha…
Read More » -
Mwambo woliza mfuti pamaliro Achingoni
Mfumu Yachingoni ikagona, pamaliropo amaomba mfuti thupi la mfumuyo lilowe m’manda. Mwezi wathawu, kudachitika maliro a T/A Bvumbwe m’boma la…
Read More » -
Umhlangano wa Maseko Ngoni lero
Kutentha masanawa kumanda kwa Gomani kwa Nkolimbo m’boma la Ntcheu pamene Angoni a m’maiko monga Zambia, Mozambique, Tanzania, South…
Read More » -
Moto buu! Ku Swaziland
Kochi wa timu ya dziko lino ya Malawi Flames, Ernest Mtawali, wati timu yake yakonzeka kuonetsa zakuda timu ya Swaziland…
Read More » -
Katundu wakwera udyo, atero anthu
Amalawi akonzekere kulira chifukwa cha kukwera udyo kwa mitengo ya zakudya ndi katundu wina komwe kwachitika kuyambira mwezi wa…
Read More » -
Muva: Kutsitsimutsa anthu mukuimba
Lero Lamulungu akuyembekezeka kukakhazikitsa chimbale chake cha Messiah 1 ku Mzuzu pa Boma Park. Kumeneko kukakhala oimba osiyanasiyana odziwika m’Malawi…
Read More » -
Abusa ku HIH ndi zina
Tsikulo ndidali pa Wenela kuitanira minibasi monga mwanthawi zonse. “Ndirande iyi! Machinjiri iyo! A Lilongwe achamba atatu iyo yopita!…
Read More » -
Anatchezera
Amandikakamiza Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 16 ndipo ndili ndi bwenzi langa la zaka 19. Iyeyu amandikakamiza kugonana naye. Ine…
Read More » -
Nyaude: Tidadabwa ndi zochitika zake
Akamaimba nyimbo ya Musalolere Mulungu Ephraim Zonda amaimba ndi mtima wonse polingalira kuti akulowa m’banja mwezi ukubwerawu ndipo Mulungu…
Read More » -
Wopezeka’ ndi yunifomu ya polisi anjatidwa
Apolisi ku Zomba akusunga m’chitolokosi bambo wa zaka 25 pomuganizira mlandu wopezeka ndi yunifomu ya polisi komanso mfuti popanda…
Read More » -
Wobwerera lili pululu amwaliranso ku zomba
ZImene zachitika m’mudzi mwa Makoloni kwa T/A Mwambo ku Zomba masiku apitawa n’zoda mutu. Mayi wa zaka 28 amene…
Read More » -
OPEZEKA KUMANDA AYANKHA MLANDU
Anthu a m’mudzi mwa Yesaya Nkosi Mfumu kwa Inkosi Chindi m’boma la Mzimba adadzidzimuka ataona galimoto yachilendo itaimitsidwa pamanda…
Read More » -
Gogo apezeka atafa atadulidwa manja, mwendo
Gogo wina wa zaka 75 wapezeka atafa m’nkhuti yokumbamo dothi loumbira njerwa m’mudzi mwa Tebulo Gondwe ku Enukweni m’boma la…
Read More » -
Pafupi mpomwe wafika?
Mkulu ali pachithunzipa mosapeneka anapanidwa ndipo apa akudzithandiza. Eetu, munthu zikakuthina upanga bwanji? Koma chodabwitsa n’choti nyumba ikuoneka kutsogolo kwakeko…
Read More » -
Moya Pete wagwa nayo
Abale anzanga, lero palibe kucheza pa Wenela. Musandifunsenso kuti chifukwa chiyani chifukwa sindingakuuzeni. Kodi simukudziwa kuti zinziri zinalowa pachipatala…
Read More » -
Zefinati Alick: Kadaulo posema ziboliboli
Aluso ndi onse koma luso losema ziboliboli si lachibwana, limafunika khama komanso munthu wolimba mtima. Pa Golomoti m’boma la Dedza…
Read More » -
anatchezera
Akuti tibwererane Anatchereza, Ndinali pambanja ndi mwamuna wa ku Nsanje ndipo ndili naye mwana mmodzi. Koma ndikati tiyeni tikaone kwanu…
Read More » -
Kudali kumapemphero a achinyamata’
Munthu aliyense ngakhale atakhala wachisodzera imakwana nthawi yomwe amayenera kusiya kusereula ndi kuchita zinthu zogwira mtima. Sam Sambo, ngakhale adali…
Read More »