Chichewa - Page 58 of 62 - The Nation Online

Category: Chichewa

JB achotsa Kachali ku EC

Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda wabweza moto, ndipo wachotsa wachiwiri wake Khumbo Kachali pampando woyang’anira bungwe la chisankho la Electoral Commission (EC).
Kapito adzudzula kukweza mitengo

Patangotha sabata bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (Mera) litakweza mitengo ya magetsi ndi mafuta agalimoto, madera ena maka kumidzi zinthu akuti zayamba kale…
Aimika malamulo a mathanyula

Mafumu ndi a mipingo ena adzudzula zomwe idanena nduna ya zamalamulo m’dziko muno, Ralph Kasambara kuti boma layamba laimika malamulo oletsa mchitidwe wa mathanyula.

Amuna ambiri amakonda zongotenga asungwana osawadziwa n’kukagona nawo ku maresitihausi. Zikatha bwino, amaoneka wochenjera. Komatu amaiwala kuti nthawi zina akhoza kugwa nazo m’mavuto oopsa.
Zokhoma pa makuponi

Ndondomeko ya fetereza wotsika mtengo [wa makuponi] chaka chino m’madera ena monga Dedza, Karonga, Zomba komanso Kasungu yatsimikizika kuti magulupu ndi nyakwawa sakulandira nawo…
Njala yavuta, mafumu achenjeza

Mafumu ena m’dziko muno apempha boma kuti liwathandize kuthana ndi njala yomwe yayamba kale kusautsa maboma angapo ndipo madera ena ayamba kale kupulumukira zikhawo.
DPP igwa pa chisankho ku Mzimba

Katswiri pa ndale, mkulu womenyera ufulu wachibadwidwe, komanso anthu ku Mzimba ati kumbwita kwa chipani cha DPP pamasankho achibwereza ku Mzimba n’chisonyezo kuti anthu…