Category: Chichewa

Kuchoka kwa Phoya kutisokoneza, atero ena

Anthu m’madera osiyanasiyana m’sabatayi ati kuchoka kwa phungu wa chipani cholamula cha DPP m’dera la ku m’mawa m’boma la Blantyre, Henry Phoya kwasiya mafunso…
Mavuto a UDF angaphe demokalase

Chipasupasu cha m’chipani chakale cholamula cha United Democratic Front (UDF) chingaopseze ulamuliro wa demokalase m’dziko muno womwe umalira kuti pakhale zipani zotsutsa zamphamvu zothandiza…