Tamvani

 • Mzimzyi kupeta mapira: Ayenera kusamala kuti kusakhale abambo

  Kucheza: Nkulakwa kupetera mwamuna

  Jul 19, 14 • Kucheza • Written by : No Comments

  Alipo amuna ambiri amene akusaukira mabanja. Akathira mbalume palibe amawalola. Ena mwa amunawa sakutha phanzi kwa asing’anga kuti akachekere mankhwala amwayi wa banja. Komatu izi akuti pena...

 • John Lanjesi (kumanja) kulimbana ndi wotseka kumbuyo wa Uganda

  ‘Agologolo’ ali pamoto mawa

  Jul 19, 14 • Masewero • Written by : No Comments

  Ulipolipo mawali pabwalo la Stade de l’Amitié ku Benin komwe Flames ikhale ikulimbana ndi kufuna kuotcha ‘agologolo’ a dziko limenelo (The Squirrels) mumpikisano wa chikho cha Afcon. Kulitu...

 • Mafumu okwezedwa ndi JB ali padzuwa

  Jul 19, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Zasolobana kumpando wa chifumu pamene mafumu ena atsopano amene adakwezedwa ndi mtsogoleri wakale Joyce Banda ayamba kuona mbonawona. Tikunenamu, mafumu akuluakulu ena alembera boma kuti lichotse...

 • Ali ku Mzuzu: 
Mkandawire (Kumanzele)

  Mizinda tsopano ili ndi mafumu

  Jul 12, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Patadutsa zaka 10 dziko lino lisadakhale ndi mafumu a mizinda, iyi tsopano ndi mbiri pamene mafumuwa abwereranso m’mizinda itatu ya dziko lino. M’sabatayi kudali kalikiliki m’mizindayi kusankha...

 • ‘Osadya za pansalu’

  Jul 12, 14 • Kucheza • Written by : No Comments

  Amuna ena ndi osusuka, amadya chilichonse ngakhale zimene zili pansalu ya munthu wamayi. Zakudya monga mtedza, chimanga ndi zina zotero akuti ndizowopsa kwa mwamuna ngati wadya. Komatu akuti nzoopsa...

 • Ngakhale patha zaka 50 zodzilamulira, sukulu zina zikuoneka ngati iyi

  Zaka 50 zaufulu

  Jul 12, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Ngakhale mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika akuti dziko la Malawi likuyenera kusangalala pa zomwe lakwanitsa m’zaka 50 za ufulu wodzilamulira, akatswiri ena kudzanso mafumu akuti zifukwa...

 • Zaka 50 taphulanji?

  Jul 11, 14 • Masewero • Written by : No Comments

  Tikusangalala kuti tatha zaka 50 tikudzilamulira. Pulezidenti Peter Mutharika akuti tisangalale koma aganyu sitikupeza chifukwa ndipo mmalo mwake tikukhuza maliro amenewa. Tisangalala bwanji pamene...

 • Gondwe: Shape your future now

  Alangiza boma pa kayendetsedwe ka chuma

  Jul 5, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Zipani zotsutsa boma ndi akatswiri pa kayendetsedwe kabwino ka boma ati boma lisamale kwambiri mmene liyendetsere ndalama zapadera zomwe aphungu a Nyumba ya Malamulo adavomereza boma kugwiritsa...

 • Chikondano: Amapatsana zinthu mwachinsinsi

  Chisiki: Mchezo wa amayi

  Jul 5, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Pamoyo wathu pali njira zambiri zomwe timalumikizirana pophunzitsana, kugawana nzeru ndi kuunikirana. Umu ndimo moyo ulili. Ngakhale izi zili choncho, ambiri amaona ngati okhala nawo pafupi ndiwo...

 • Chekucheku: Sindichoka ufumu mpaka nditafa

  ‘Chekucheku kuno ayi’

  Jul 5, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Chigamulo pamwamba pa chigamulo. Patangotha sabata imodzi bwalo lalikulu lamilandu mumzinda wa Blantyre litabwezeretsa T/A Chekucheku wa m’boma la Neno pampando, anthu ena m’bomali ati...