Dikirani kauniuni wachiwiri wa mbewu
Unduna wa za malimidwe wati anthu asathyolere khosi zotsatira za kauniuni woyamba wa mbewu chifukwa kauniyo sadalingalire za ng'amba yomwe...
Unduna wa za malimidwe wati anthu asathyolere khosi zotsatira za kauniuni woyamba wa mbewu chifukwa kauniyo sadalingalire za ng'amba yomwe...
Mamembala ena a chipani cha Malawi Congress (MCP) akutsutsana ndi maganizo amene komiti yaikulu ya chipanicho (NEC) idamanga kumsonkhano wake....
A Chimwemwe Zololo atha masiku 6 m’chitokosi cha apolisi ku Zomba powaganizira kuti amafuna kugulitsa mwana wompeza. A Zololo akuyembekezereka...
Mwana wa zaka 15 ali m’manja mwa apolisi ku Mangochi pomuganizira kuti adazimitsa mchemwali wake wa zaka 26 pa mkangano...
Walira mvula waliranso matope. Anthu amene amalakalaka atapeza chiphaso cha unzika mwayi wawagwera koma ayenera akhetse thukuta kuti izi zitheke....
Akatswiri pa nkhani za chuma ndi ufulu wa anthu adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kaamba kolephera kukwaniritsa...
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latsutsa mphekesera yoti layamba laimika kaye chilinganizo choonjezera madera a aphungu pa...
Chaka cha 2023 chikupita ndi nkhani zake, imodzi mwa nkhani zimene zidayala nthenje ndi ya msungwana wa zaka 14 yemwe...
Mkazi wa Inkosi ya Makhosi Gomani V, Inkosikati Rishaladza Khanyisa Gomani wati kuchuluka kwa mimba za ana achichepere kukukolezera kusachita...
Apolisi amanga anthu 6 omwe akuwaganizira kuti adatengera lamulo m’manja mwawo potengapo gawo pa kuphedwa kwa abambo 4 omwe amaganiziridwa...
Nduna ya za chitetezo cha m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma ati unduna wawo wakhwimitsa chitetezo m’nyengo ya zisangalalo za Khrisimasi...
Woweruza ku bwalo la milandu lalikulu ku Lilongwe a Justice Howard Pemba ati adzapereka chigamulo chawo pa 26 December 2023...
Pamene bwalo lina ku Zomba m’sabata yangothayi lidagamula kuti mphunzitsi wina ndi wosalakwa pa mlandu wogwiririra mwana wophunzira pasukulu ya...
Nduna ya za chitetezo cha m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma ati pofika m’chaka cha 2025 pomwe Amalawi adzaponye voti ya...
Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Peter Mutharika wauza mamembala omwe sakumumvera m’chipanicho kuti achoke asaononge chipani. A...
Amfumu a Chidzalo a zaka 71 omwe dzina lawo ndi a Moffat Lamulani Mlenga a m’boma la Dowa adzikhweza pothawa...
Apolisi ku Ntchisi amanga anthu 10 a m’mudzi mwa Kanyenda kwa T/A Kalumo potsatira mkangano wa ufumu pakati pa a...
Mayi wa zaka 19 wadzipha ku Kasungu atazindikira kuti mwamuna yemwe adakwatirana naye pokhulupirira kuti banja lake loyamba lidatha ndi...
Pakati pa usiku wa Lachitatu sabata yatha, ndalama ya kwacha idatsika mphamvu ndi K44 pa K100 iliyonse. Izi zachititsa kuti...
Chiwanda chachilendo chophana m’mabanja chalowerera moti mwezi umodzi okha, bambo wina ku Zomba adapha mkazi wake, banja lina ku Chiradzulu...