Uchikumbe

 • Alimi ena akusosa

  Jun 28, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Mchikumbe sapuma pantchito ya kumunda chifukwa imakhala ikupitirira chaka chonse. Nthawi ino pomwe zokolola zachotsedwa m’minda n’kofunika kuti alimi ayambe kukonzekera ulimi wa chaka chino....

 • Adandaula ndi mitengo ya mbatata

  Jun 28, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Alimi ku Mchinji agundika kulima tomato wa kudimba pofuna kupha makwacha ndi tomato wamthirira uku akufufuza misika ya mbewu zakumunda. Alimi ambiri amakonda kulima tomato wachilimwe pogwiritsa...

 • Kulibe tchuthi kwa mlimi

  Jun 28, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Alimi ambiri akolola ndipo alimi ozindikira akudziwa kuti palibe nthawi yopuma poti akuyenera kutembenukira kuulimi wa kudimba. Alimi ambiri m’madera a boma la Lilongwe ayamba ntchitoyi ndipo...

 • Adandaula ndi mitengo ya mbatata

  Jun 28, 14 • Nkhani • Written by : No Comments

  Chongofika pamsika wa Chinakanaka m’boma la Mulanje, matumba ochuluka a mbatata amaoneka. Mwina n’kumati, apa ndiye pali kupha makwacha. Koma ayi, thumba limodzi la mbatata lokhala ndi chimuni...

 • Mtalimanja-rice-project

  Kuli kholola la mnanu la mpunga

  Jun 13, 14 • Career Of The Week, Nkhani • Written by : No Comments

  Kuli dzinthu chaka chino. Pali chiyembekezo kuti alimi ampunga akolola zochuluka kaamba ka njira yamakono yochulukitsira mpunga. Njirayi, yomwe ikutchedwa System of Rice Intensification (SRI),...

 • Boma lati chaka chino zokolola zachuluka

  Kuli dzinthu—Unduna

  May 17, 14 • Nkhani • Written by : Comments Off

  Unduna wa za ulimi ndi kuonetsetsa kuti m’dziko muno muli chakudya chokwanira watulutsa zolosera za kholola wa chaka chino zomwe zasonyeza kuti kuli dzinthu zamnanu. Zomwe undunawu watulutsa,...

 • Alimi awalimbikitsa kukonza ndondomeko

  May 10, 14 • Nkhani • Written by : Comments Off

  Pomwe ntchito za ulimi wa chaka chatha zikupita kumapeto, nthambi ya zaulimi ya Lilongwe ADD yapempha alimi kuti ayambe kukonza ndondomeko za mmene ayendetsere ulimi wa chaka chino. Mkulu woyendetsa...

 • Zakudya zamtchire nzothandiza kuthanzi

  May 10, 14 • Nkhani • Written by : Comments Off

  Papita zaka 2 500 kuchokera pamene wotchuka wina odziwika ndi ndidzina lakuti Hippocrates adalengeza kuti: “Chakudya chikhale mankhwala anu komanso mankwala akhale chakudya chanu.” Zimene...

 • Kukonzekera ulimi wamthirira n’kofunika

  Ayamba kukonzekera ulimi wa mthirira

  Apr 19, 14 • Nkhani • Written by : Comments Off

  Alimi achangu ayamba kale kukonzekera ntchito za ulimi wamthirira wa chaka chino ngakhale kuti mbewu zina zikadali m’minda. Mlimi wa chitsanzo wochokera ku Kasungu, Paulo Phiri, wati alimi omwe...

 • Perekani mitengo yoyenera kwa alimi: Banda pamene ankatsekulira msika wa fodya ku Kanengo, Lilongwe

  Msiska wa fodya wayamba bwino

  Mar 29, 14 • Nkhani • Written by : Comments Off

  Alimi a fodya ali ndi chiyembekezo choti apha makwacha ochuluka chaka chino ngati mitengo yomwe ogula mbewu akupereka kuokushoni ingapitirire kapena kukwera kuposa apa. Potsegulira malondawa Lolemba...