-
Nkhani
Chitetezo chalowa nthenya m’malawi
Chitetezo m’dziko muno chaphwasuka. Anthu akuyenda mwamantha pamene ena akuphedwa komanso katundu akubedwa molapitsa. Sabata yangothayi, zigawenga 8 zakhapa mfumu…
Read More » -
Mafumu okwezedwa ndi JB ali padzuwa
Zasolobana kumpando wa chifumu pamene mafumu ena atsopano amene adakwezedwa ndi mtsogoleri wakale Joyce Banda ayamba kuona mbonawona. Tikunenamu, mafumu…
Read More » -
Nkhani
Mizinda tsopano ili ndi mafumu
Patadutsa zaka 10 dziko lino lisadakhale ndi mafumu a mizinda, iyi tsopano ndi mbiri pamene mafumuwa abwereranso m’mizinda itatu ya…
Read More » -
Nkhani
Zaka 50 zaufulu
Ngakhale mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika akuti dziko la Malawi likuyenera kusangalala pa zomwe lakwanitsa m’zaka 50 za ufulu…
Read More » -
Nkhani
‘Chekucheku kuno ayi’
Chigamulo pamwamba pa chigamulo. Patangotha sabata imodzi bwalo lalikulu lamilandu mumzinda wa Blantyre litabwezeretsa T/A Chekucheku wa m’boma la Neno…
Read More » -
Nkhani
Mamulumuzana agwa
Chisankho chapatatu chadza ndi zowawa zake. Pamene mpando wa pulezidenti wakhala wokokerana, mipando ya aphungu nayo yagwetsa mamulumuzana. Omwe ndi…
Read More » -
Editors Pick
NGO promotes savings culture in Blantyre
A Blantyre-based non-governmental organisation, A Self-Help Assistance Programme (ASAP), has urged communities to adopt and popularise the culture of saving…
Read More » -
Nkhani
Mfundo mbweee kumtsutso
Makandideti 11 amene adasonkhana ku mtsutso wa atsogoleri usiku wa Lachiwiri m’sabatayi alonjeza zodzasintha moyo wa anthu akumudzi ngakhale makandidetiwa…
Read More » -
Akufuna T/A Chekucheku achoke
Anthu okwiya Lolemba ndi Lachiwiri m’sabatayi adasonkhana paofesi ya DC wa boma la Neno komwe amapempha bwanamkubwayo kuti achotse T/A…
Read More » -
Bambo wa mitala apumira pambuzi
Mbuzi zadya malo. Patangotha miyezi iwiri mkulu wina ku Nkhotakota atachita chisembwere ndi mbuzi, bambo winanso wamitala ndipo ali ndi…
Read More » -
Nkhani
Zimbalangondo zikhapa achitetezo
Anthu akugona khutu lili kunja, tulo tayamba kusowa, chitetezo chatekeseka ku Soche mumzinda wa Blantyre komwe zimbalangondo zatikita achitetezo a…
Read More » -
Nkhani
Mafumu atekeseka ndi bilu ya malo
Mafumu ena m’dziko muno aopseza kuti achita zionetsero ngati lamulo lokhudza malo lingasinthe kuti iwo asakhalenso ndi mphamvu pogawa malo.…
Read More » -
National News
abortion scourge:Hospital registers 51 cases in three months
She is making a killing—literally—through conducting abortions in Mtakataka in Dedza, leaving three girls in serious condition after ‘operations’ went…
Read More » -
National News
Famers should wait for biotechnology crops
Principal of Bunda College of Agriculture of the Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar), Professor Moses Kwapata, has…
Read More » -
Nkhani
Mashado a PP ndiwo agawe chimanga cha boma
Anthu amene satsatira chipani cha PP ali pachiopsezo chosumbudzuka ndi njala pamene boma lauza mashado a PP kuti ayambe kugawa…
Read More » -
National News
Thugs hunt Godknows Maseko
The life of the executive director for Step Kids Awareness (Steka), Godknows Maseko is in danger after five unknown thugs…
Read More » -
National News
48 caregivers trained in Mdeka
Lighthouse Foundation (LHF)— a Korean non-government organisation—on Friday awarded certificates to 48 caregivers in Traditional Authority (T/A) Chigaru in Blantyre.…
Read More » -
Editors Pick
When football turns into death trap
It was devastating and traumatising for the 23-year-old woman who was brought into the Balaka District Hospital mortuary to identify…
Read More » -
Chichewa
‘Kudali ku Namiwawa CDSS’
DJ Khumbo ndi mmodzi mwa anyamata odziwika bwino pankhani yotembenuza zimbale kuti anthu azivina. Iye amatembenuza zimbale monga DJ ndi…
Read More » -
Chichewa
Bwanji wodwala chikuku amasamalidwira kutchire?
Makono ano munthu wodwala chikuku amasamalidwa pakhomo kapena kuchipatala ndipo malangizo amene kale ankatsatidwa adalekeka. Kalelo, wodwala chikuku ankakabisidwa kunkhalango…
Read More »