Minister vows to punish errant contractors

Minister of Gender, Children, Disability and Social Welfare Mary Navicha has warned that her ministry will punish contractors that construct government buildings that are inaccessible to people with physical disabilities. The minister said this on Wednesday during the commemoration of International Day of Persons with Disability at Chileka in Blantyre. Navicha said that although there…

Crop diversification could end hunger—Minister

Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development Kondwani Nankhumwa has asked farmers in the country to diversify their farming to combat malnutrition and hunger. The minister said this on Wednesday during the commemoration of this year’s World Food Day at Kankhomba Primary School in Thyolo where he was the guest of honour. The theme for…

Tetezani ana ku BP

Chimodzimodzi akulu, ana nawo amakhala pachiopsezo cha matenda othamanga magazi choncho makolo akuyenera kuwateteza, watero mkulu wa pa chipatala cha Moyowathanzi m’boma la Lilongwe Henry Ndhlovu akuti. Iye adafotokoza kuti ana omwe amakhala pa chiopsezo chodzadwala matendawa mtsogolo ndi oyambira zaka zitatu kulekezera 6 kapena 8. “Kawirikawiri ana oterewa amakhala omwe adabadwa masiku asadakwane komanso …

Samalani ndi chitopa

Kuchokera ku phindu la ulimi wothirira, Catherine Bamusi wa m’boma la Blantyre adaganiza zogulako nkhuku zachikuda kuti zizimupatsa manyowa, ndiwo ngakhalenso ndalama akazingwa. Iye adayamba ndi nkhuku 6 chaka chathachi ndipo pamene amalowa m’chaka chino zidali zitachulukana kufika 50. “Ndili mkati modyerera, nkhuku zanga zidagwidwa ndi chitopa ndipo padakalipano ndilibe ndi imodzi yomwe chifukwa zonse…

Akupha makwacha ndi nkhumba

Pamene alimi ena akugulitsa ziweto zawo kwa mavenda motsika mtengo, Chawezi Nyirenda yemwe ndi mlimi wa nkhumba ku Lilongwe akupha makwacha a nkhaninkhani popha khumba zake zikakula, kuzikonza mopatsa kaso n’kumagulitsa yekha. ESMIE KOMWA adacheza naye motere: Kodi chidakuchititsani kuti muyambe kukonza nyama ya nkhumba zanu n’kumagulitsa nokha n’chiyani? Nditakhala pansi n’kulingalira mozama ndidaona kuti…

Muli mphamvu mu ukhondo

Bungwe la Water for People Malawi (WPM) lomwe cholinga chake n’kuonetsetsa kuti anthu m’dziko muno azimwa madzi aukhondo, komanso kukhala ndi zimbudzi zabwino lati mu ukhondo muli mphamvu chifukwa munthu sadwaladwala choncho amagwira ntchito molimbika. Bungweli layankhula izi Lachiwiri ku Chiradzulu pa mwambo wosayinirana ndondoneko za ntchito za ukhondo ndi khonsolo ya m’bomalo. Malingana ndi…

Kupewa chigodola cha nkhumba ndikotheka

M’mwezi wa February chaka chino mlimi wina wa nkhumba m’boma la Lilongwe, Jeofrey Kaiyatsa, adaona ngati malodza nkhumba zake zonse zitafa ndi chigodola. Panthawiyo n’kuti ali ndi nkhumba zazikulu zosachepera 30. Funso n’kumati: kodi zidamuvuta pati? “Ndikuganiza kuti mnyamata yemwe ndidamulemba ntchito yosamalira nkhumbazi samayenda bwino choncho adakatenga matendawa kwina n’kulowetsa m’makola. “Ku Lilongwe kuno…

Ulimi wa njuchi ndi ofesi yonona

Kodi ulimi wa njuchi mudayamba liti? Ulimiwu ndidayamba mu 2017. Nanga chidakukopani n’chiyani? Nditalingalira mozama ndidaona kuti ulimi wa njuchi sulira zinthu zambiri monga kulima, kugula feteleza, mankhwala ndi zina zochuluka kuti utheke. Chinthu china chomwe chidandikopa n’choti anthu masiku ano akukonda kugwiritsa ntchito uchi ngati chotsekemeretsa kusiyana ndi shuga malingana ndi zovuta zosiyanasiyana za…

Sungani mbatata m’munda,  M’nkhuti kuti isaonongeke

Alfred Mumba wa m’boma la Dowa  amalima mbatata pa malo okwana maekala 5. Iye amapeza matumba osachepera 250 a mbatata pachaka kuchokera pa malowa koma chomvetsa chisoni n’choti amangokwanitsa kugulitsa theka lokha la zokolola zake. “Ndikanyamula matumba 10 kupita nawo ku msika, 5 okha ndiomwe ndimagulitsa pa mtengo  wabwinoko ndipo osalawo, ndimagulitsa mongotaya kapena kungozisiya…

Project to improve hygiene, increase access to water in CZ

Water for People Malawi (WPM) and Chirazulu District Council have signed a three-year memorandum of understanding (MoU) that will see the organisation implementing water, sanitation and hygiene (Wash) interventions in the district. Speaking during the signing ceremony on Tuesday, WPM country director Kate Harawa said the organisation has put aside K2.5 billion for the project.…

Osaiwala kuteteza mtedza ku chuku

Pamene mbewu ya mtedza yacha, katswiri wa mbewu za mtunduwu kwa Bvumbwe Richard Andasiki akuti alimi ateteze mbewuyi ku chuku pamene akukolola, kuyanika, kusenda komanso kusunga. Malinga ndi katswiriyu, mtedza umachita chuku mlimi akafulumira kapena kuchedwa kukolola, ukanyowa poyanika, mlimi akauviika m’madzi ndi cholinga choti asende mosavuta kapena akasunga pachinyontho. “Tisaiwale kuti tikapitiriza kukhala ndi…

Mafizo amathandiza anthu achikulire

Woona za mafizo pa chipatala cha anthu achikulire cha Kalibu ku Lilangwe m’boma la Blantyre Veronica Mughogho akuti mafizo ndiothandza kwambiri pa miyoyo ya anthu osachepera zaka 60. Mughogho adati mafizo amathandiza anthu a misinkhuyi kuti asakalambe msanga komanso  kupewa mavuto ndi matenda osiyanasiyana omwe amadza kaamba ka ukalamba. “Mafupa komanso mokumanira mwake mumalimba bwino…

Zinthu zitatu mu nkhuku imodzi ya Mikolongwe

Katswiri wa ulimi wa ziweto wa ku Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar) Timothy Gondwe wati kukhala ndi nkhuku ya Mikolongwe imodzi ndi chimodzimodzi kukhala ndi nkhuku zitatu—yanyama, yachikuda ndi yamazira. Iye adati nkhuku ya Mikolongwe imakula kwambiri, imaikira mazira ambiri, komanso kukoma kwa mazira ndi nyama yake ndi chimodzimodzi nyama ndi mazira…

Tigwirane manja pothana ndi chisaka cha Nthochi

Mkulu woona za mbewu za m’gulu la zipatso ku dipatimenti ya za kafukufukuku mu unduna wa zamalimidwe Felix Chipojola akuti nkhondo yolimbana ndi matenda a chisaka cha nthochi m’dziko muno siingaphule kanthu pokhapoka anthu atagwirana manja. Iye adafotokoza kuti njira yokhayo yothana ndi chisaka ndikuchotsa nthochi zonse zakale ndikubzala zina. Chipojola adati m’zomvetsa chisoni kuti…

Akangalika ndi ulimi wa mthirira

Mlimi wochenjera monga NELLIE NYONI wa m’boma la Balaka amayambiratu ulimi wa m’chilimwe mvula ikamapita kumapeto kuti asavutike kwambiri ndikuthirira. Tikunena pano adabzala kale chimanga komanso nyemba  ndipo posachedwapa ziyamba kubereka. ESMIE KOMWA adacheza ndi mlimiyu motere: Kodi n’chifukwa chiyani mumafulumira kuyambapo ulimi wa mthirira? Choyambirira ndimafuna kuti ndigwiritse ntchito chinyezi chochuluka chomwe chimapezeka mvula…

Gwiritsani bwino ntchito chinyezi kuti mupindule

Potsatira mvula yochuluka yomwe yagwa m’chakachi, akatswiri a za kafukufuku wa ulimi wa mthirira  akuti alimi a m’zigwa za dziko lino, m’mbali mwa mitsinje komanso omwe ali ndi madambo agwiritse ntchito chinyezi kulima mbewu zosiyanasiyana ndipo aphula kanthu. M’modzi mwa akatswiriwa, Isaac Fandika wa ku Kasinthula Research Station m’boma la Chikhwawa adati madera monga a…

Tikolole motani chimanga?

Alimi m’madera a dziko lino amakolola chimanga mosiyanasiyana malingana ndi kuzolowera kwawo koma mphunzitsi wa kunthambi ya za maphunziro a za ulangizi ku Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar) Paul Fatch akuti njirazi zili ndi ubwino ndi kuipa kwake. Chachikulu, iye adati mlimi amayenera kukonzekera kuthana ndi zinthu zomwe zikhoza kudza kaamba ka…

Chenjerani pokolola

Mbewu ya chimanga nayo imafuna kuyichengetera nthawi yokolola kuti zokolola zikhale zochuluka ndi zopatsa kaso. Wachiwiri kwa mkulu woona za kafukufuku wa mbewu ku Bvumbwe Research Station, Frank Kaulembe akuti nankafumbwe amaononga ngati alimi akolola chimanga chawo mochedwa kapena mofulumira. Mwachitsanzo, iye adati kukolola mbewuyi isadaume,  mlimi akaiyanika imafota ndipo zotsatira zake nankafumbwe amaboola mosavuta.…

Women farmers should  access loans–UN Women

United Nations (UN) Women  has moved to lobby for rural women farmers’  access to loans from financial institutions. Speaking yesterday during a round table meeting that attracted various agricultural stakeholders, micro-finance institutions (MFIs)and rural women farmers in Blantyre, UN Women Malawi representative Clara Anyangwe said they wanted to provide a platform for discussing issues pertaining…

Zizindikiro za kufa kwa ziwalo

Dotolo wa pa chipatala cha Gulupu m’boma la Blantyre, Lerato Mambulu, wati kufa kwa ziwalo nthawi zambiri kumachitika mwadzidzidzi. Pachifukwa ichi, kumakhala kovuta munthu kumva kapena kuonetsa zizindikiro zoti afa ziwalo. “Munthu amatha kungomva kupweteka mutu ngati amumenya mwina ndi chitsulo ndikugwa pansi basi kufa kwa ziwalo n’kukhala komweko,” iye adatero. Mambulu adafotokoza kuti izi…

Powered by