Imfa ya Chikulamayembe yautsa mapiri pachigwa

Mkangano wabuka m’banja la a Gondwe pa za munthu yemwe akuyenera kulowa ufumu wa Chikulamayembe. Mpungwepungwewu wayamba potsatira imfa ya Walter Gondwe, yemwe adali mfumu Chikulamayembe. Mfumu Chikulamayembe idamwalira pa November 29 2018. Isadamwalire idasankhiratu mwana wake, Mtima Gondwe, kuti ndiye adzalowe ufumu wake ndipo mafumu ena adavomera n’kusainira panganoli ndi Chikulamayembe asadatsikire kulichete. Koma…

Voting faces hitches in  Mzimba, Mzuzu City

  Presiding officers in Mzimba and Mzuzu City struggled to with the electronic voting system, leading to delays in transmitting election results of the May 21 Tripartite Elections. By 5:30pm yesterday, most centres had not done half of the results transmission due to irregularities arising from the presiding officers handling of paperwork. Mzimba district commissioner…

MEC reminds voters of polling procedure

With only a day to go before the tripartite elections, the Malawi Elections Commission (MEC) has reminded all registered voters on the polling procedure. About 6.9 million Malawians registered to cast their votes to choose councillors, members of Parliament and a president. MEC’s director of media and public relations Sangwani Mwafulirwa said in an interview…

Women embrace climate smart agriculture

Women from Ntchenachena and Chiweta in Rumphi have embraced climate smart agriculture to increase their yields.   Mphizi Women Club chairperson Maggie Gondwe has since asked Civil Society Network On Climate Change (Cisonecc) for more support because the varieties are on high demand in the area. “We have a huge seed market here because most…

More firms seek MBS certification

Malawi Bureau of Standards (MBS) says many companies are now seeking standardisation and quality assurance from the institution. MBS director general Symon Mandala said this in Mzuzu on Friday during a certification awards presentation. He said the number of firms seeking services of MBS have jumped from 645 in December last year to 701 this…

‘Ndidamuona koyamba mu Shoprite’

Kwangotsala sabata ziwiri zokha kuti anthu adzathyole dansi paphwando la ukwati wa Evance Mwale ndi Tiwonge Nundwe pa 4 May. Evance amagwira ntchito ku Sinodi ya CCAP ya Livingstonia pomwe bwenzi lakelo ndi muulutsi pa wailesi ya Voice of Livingstonia. Awiriwa akhala pa ubwenzi kwa zaka zitatu. Malinga ndi Mwale, adamuona koyamba Nundwe mu Shoprite…

Rumphi man plants 43 000 trees

Golden Mlowoka Chirwa, a resident of Mphompha in Rumphi, has planted 43 000 blue gum tree seedlings in the just ended tree planting season to mitigate effects of climate change. The man is a beneficiary of Mzuzu-based Wells of Zoe, a non-governmental organisation (NGO) which encourages people in rural communities to invest in trees to…

Comsip trains productive asset transfer beneficiaries

Community Savings and Investment Promotion (Comsip) Cooperative Union Limited has trained 50 asset transfer beneficiaries in management of various businesses to ensure sustainable income. With funding from the World Bank, the five-day training, which started on Wednesday, aims at moving these households away from consumption and idle labour to more productive self-employment. Comsip business and…

‘Amayi oyembekezera akulipira k10 000’

Kusamvana kwabuka pachipatala cha chaching’ono cha Chikangawa m’boma la Mzimba pamene amayi oyembekezera akulipiritsidwa K10 000 pokabereka. Amayiwo omwe auza Msangulutso ati ndi odabwa kuti mwana akangobadwa, achipatala akumalamula kholo lake kuti lilipire K10 000. “Kulibe komwe tingathawire, chipatala chathu ndi chimwechi, sitikudziwa ngati boma lakhazikitsa malamulo woti tiyambe kulipira m’zipatala tikakabereka. Kudabwitsa kwake sakumatipatsa…

Malawi loses out  on k885bn market

Local producers are failing to take advantage of $1.2 billion (about K885 billion) market for various agricultural products due to low output, a development Malawi Investment and Trade Centre (Mitc) says is worrisome. The commodities include chillies, rice, beans, soya, groundnuts, macadamia, honey, sunflower and cotton seed, according to Mitc. Mitc director of investment, promotion…

Teveta trains 30 mastercraft persons in bakery, pastry

Technical, Entrepreneurial, Vocational Education and Training Authority(Teveta) says there are critical skills gaps in pastry and bakery in the country. Speaking during a baking and pastry training graduation in Mzuzu, the authority’s acting director of quality assurance Charles Mataya Phiri said to address such gaps, the authority, in conjunction with Mzuzu University (Mzuni), has trained…

Abwatika bwalo,  Polisi ku mangochi

Fisi adakana msatsi. Mayi yemwe adauza abale kuti mwamuna wake amafuna kugulitsa mwana wawo wa chialubino wasintha Chichewa. Vanessa Manyowa wauza bwalo la milandu ku Mangochi kuti zomwe adanenazo zidali zopeka chifukwa panthawiyo n’kuti atayambana ndi mwamuna wake pa nkhani za kumunda. Mayiyo adabereka mwanayo wa chialubino asadakwatiwe ndi mwamuna wake watsopanoyu. Padakali pano mwanayo…

Akhutira ndi mitsutso ya atsogoleri  andale

Akatswiri andale akhutira ndi mitsutso ya atsogoleri omwe akudzaima nawo pa zisankho zapatatu zomwe zichitike m’dziko muno pa May 21 chaka chino. Akatswiriwa ati mitsutsoyi ndi yofunika kwambiri pa ndale za demokalase kaamba koti imapereka mwayi kwa atsogoleri wotambasula mfundo zawo za chitukuko. Iwo adati chokondweretsa n’choti anthu akupatsidwa mwayi wofunsa pamene sakumvetsetsa. Mmodzi mwa…

Boma likweza aphunzitsi 20 210

Bungwe la aphunzitsi m’dziko muno la Teachers Union of Malawi (TUM) lati ndilokondwa ndi kukwezedwa kwa aphunzitsi 20 210 a m’sukulu za pulayimale ndi sekondale. Anthu ena akuti boma la DPP lachita izi pofuna kukopa aphunzitsi kuti adzachivotere pa zisankho zapatatu zomwe zidzachitike m’dziko muno pa May 21. Boma lidakweza aphunzitsi kotsiriza m’chaka cha 2013…

Parties dared on funding

Centre for Multiparty Democracy (CMD) has challenged political parties contesting in the May 21 2019 Tripartite Elections to disclose sources of their funding in accordance with the Political Parties Act. Speaking in Mzuzu on Friday when Malawi Electoral Commission (MEC) launched a voter education campaign, CMD executive director Kizito Tenthani said disclosure of sources of…

Masalamusi asokoneza maphunziro ku Lunzu

Sukulu ya sekondale ya Lunzu mu mzinda wa Blantyre idatsekedwa kwa sabata imodzi kaamba ka masalamusi omwe amachitikira atsikana pa sukulupo. Msangulutso wauzidwa kuti atsikana kuti atsikana apasukuluyi amadzipindapinda modabwitsa ndipo akafunsidwa, amayankha kuti akumva kupweteka muti ndi m’thupi.  Chodabwitsa nchoti atapita nawo ku chiatala, madotolo sadawapeze ndi matenda aliwonse. Izi zidachititsa unduna wa maphunziro…

Achikulire asowa thandizo madzi atavuta

Limodzi mwa mabungwe omenyera ufulu wa anthu achikulire m’dziko muno lati ena mwa achikulire amene adakhudzidwa ndi madzi osefukira sabata ziwiri zapitazo sakulandira thandizo loyenera kuchokera ku boma. Madzi osefukirawa akhudza maboma 15 mwa 28 m’dziko muno, ndipo anthu 868 895 ndiwo akusowa pokhala chifukwa cha vutoli. Mwa anthuwa, 672 ndiwo adavulala pomwe 56 adaphedwa,…