Nkhani
-
Adzudzula woswa mkazi ndi njerwa
yomwe ili m’dziko muno yomwe mtsogoleri wa dziko a Lazarus Chakwera adalengeza kuti yakhudza kwambiri maboma 23 mwa maboma 28…
Read More » -
Sinodi ya Livingstonia ayisambira m’manja
Likulu la mpingo wa Church of Central African Presbyterian (CCAP) la General Assembly lati sililowerera pa kusemphana komwe kwabuka mu…
Read More » -
Apempha a Chaponda kuganizira Amalawi
Atatengetsa boma pa nkhani yokhudza lipoti la ngozi ya ndege Lachiwiri m’Nyumba ya Malamulo, mtsogoleri wa otsutsa boma m’nyumbayo a…
Read More » -
Adzudzula MEC
Magulu osiyanasiyana okhudzidwa ndikayendetsedwe kazisankho adzudzula bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) posintha masiku odzachita kalembera wa kaundula…
Read More » -
Tikumafa nthawi ya chisankho achialubino adandaula
Anthu ambiri m’dziko muno akugwedezabe mitu ndi nkhani yomwe inachitika ku Kasungu. Kumeneko, apolisi anamanga mayi wina yemwe amachokera m’mudzi…
Read More » -
Woganiziridwa kuzembetsa anthu wagwidwa
Mwambi woti khoswe wa pa tsindwi adaulula wa pa dzala wapherezera ku Mulanje komwe mlandu wa pa msewu wavumbulutsa mulandu…
Read More » -
Msonkhano wa UTM walephereka
Msonkhano womwe komiti yaikulu ya chipani cha UTM imayenera kukhala nawo walephereka. M l e m b i w a…
Read More » -
Musandinjate, ndinali ku ndende komweko
A Jonathan Ng’ambi Lachinayi sabata yatha adaseketsa omvera milandu m’khoti la Chitipa atapempha woweruza milandu kuti asawapititse ku ndende ati…
Read More » -
Ozunza mwana avomera mlandu
Bwalo la milandu ku Balaka lati pa 18 July lidzapereka chilango kwa mayi Lilian Matako omwe Lachisanu adavomera mlandu woti…
Read More » -
Woima ndi pulezidenti azikhala wotani?
Mwezi wa June 2025 onse ofuna kudzapikisana nawo pa chisankho cha Pulezidenti adzakhala akupereka kalata zawo ku bungwe la Malawi…
Read More »