Nkhani
-
Anthu alembetsa mwaunyinji—MEC
Bungwe loyendetsa zisankho la MEC lati anthu chiwerengero cha anthu omwe alembetsa kuti adzavote pa Chisankho Chachikulu cha pa 16…
Read More » -
Amuna anga matama thooo!
Azakhali, zili kwathu simungazimvetse. Ife tonse tili pa ntchito. Tonse timalandira ndalama zokwanira ndithu. Komwe ndalama za amuna anga zimapita…
Read More » -
‘Samalani m’masamba a mchezo’
Mkulu wa bungwe loteteza ufulu wa ana ndi achinyamata a MacBain Mkandawire wapempha Amalawi kuti azigwiritsa ntchito masamba a mchezo…
Read More » -
America iyimika thandizo
Kadaulo wa mgwirizano wa mabungwe a zaumoyo la Malawi Health Equity Network (Mhen) a George Jobe ati zomwe lachita dziko…
Read More » -
Mtengo wa chimanga wapenga
Kusowa kwa chimanga m’misika ya Admarc kwapereka danga kwa mavenda ogulitsa chimangacho kuti akame Amalawi omwe akulira kale ndi njala…
Read More » -
Ati tikhwimire mwana
Ndili pa banja ndipo tili ndi ana angapo. Banja lathu ndi loopa Mulungu. Ndipo tonse ndi atsogoleri ku mpingo wathu.…
Read More » -
Banja lituluka pa belo
Bwalo la milandu mu mzinda wa Blantyre, Lachisanu lidapereka belo kwa mayi Linda Chitala ndi amuna awo a Macferson Chitala…
Read More » -
Akuluakulu 6 amangidwa m’masiku awiri
Akuluakulu omwe akudzimva fungo la milandu akuyenera kuyenda cheucheu kaamba koti unyolo wathyola mpanda ku polisi ndipo ukuika manja kumbuyo…
Read More » -
APM adzudzula Chakwera
Kadaulo pa ndale a George Phiri wati akugwirizana ndi zimene adanena mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika kuti…
Read More » -
Ndimamufuna kwambiri
Anatchereza M’mudzi mwathu mudabwera mtsikana wina wake yemwe ndidakondweretsedwa naye. Ndidachita machawi kumufunsila ndi kumuuza kuti ndimamukonda koma sadandiyankhe. Mwa…
Read More »