Chichewa

Pafupi mpomwe wafika?

Listen to this article

pee

Mkulu ali pachithunzipa mosapeneka anapanidwa ndipo apa akudzithandiza. Eetu, munthu zikakuthina upanga bwanji? Koma chodabwitsa n’choti nyumba ikuoneka kutsogolo kwakeko ndi nyumba yaikulu (chimbudzi) yomwe idamangidwa ndi cholinga choti anthu ngati, mnzathuyu, azikadzithandiziramo akapanikizika, koma ayi ndithu, akuti pafupi mpomwe wafika. Mizinda ndi matauni athu ukhondo ukusowekera chifukwa cha mchitidwe ngati umenewu. Payenera kukhala malamulo, ngati mmene zilili kumaiko ena, kuti anthu otere azimangidwa akapezeka kuti akumadzithandizira paliponse.—Joseph-Claude Simwaka

Related Articles

Back to top button