Amanga 10 pa mkangano wa ufumu
Apolisi ku Ntchisi amanga anthu 10 a m’mudzi mwa Kanyenda kwa T/A Kalumo potsatira mkangano wa ufumu pakati pa a...
Apolisi ku Ntchisi amanga anthu 10 a m’mudzi mwa Kanyenda kwa T/A Kalumo potsatira mkangano wa ufumu pakati pa a...
Mayi wa zaka 19 wadzipha ku Kasungu atazindikira kuti mwamuna yemwe adakwatirana naye pokhulupirira kuti banja lake loyamba lidatha ndi...
Pakati pa usiku wa Lachitatu sabata yatha, ndalama ya kwacha idatsika mphamvu ndi K44 pa K100 iliyonse. Izi zachititsa kuti...
Chiwanda chachilendo chophana m’mabanja chalowerera moti mwezi umodzi okha, bambo wina ku Zomba adapha mkazi wake, banja lina ku Chiradzulu...
Nthambi ya za nyengo ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati kutentha kwa mnanu komwe kwakhala kuoneka...
Asungwana 5 600 omwe akadalephera sukulu kaamba ka vuto la fizi achita mwayi ndi lonjezo la bungwe la United Nations...
Akadaulo pa nkhani zosiyanasiyana m’dziko muno ati mbali yotsutsa boma ili ndi benthu lake pa mavuto omwe Amalawi akudutsamo chifukwa...
Khoti la majisitileti m'boma la Dowa lamanga mbusa wina Bonwell Sinoya wa zaka 36 kukagwira ntchito yakalavula gaga kwa zaka...
Vuto la mafuta a galimoto lomwe lanyanya tsopano lakweza mkwiyo mwa Amalawi kaamba kakukwera kwa mtengo wa galimoto zonyamula anthu...
Thupi la mphangala pa ndale a John Tembo lidalowa m’manda Lachitatu ku mudzi kwawo kwa Kaphala kwa T/A Kachere ku...
Kadaulo pa za chitetezo a Loti Dzonzi omwe adakhalako mkulu wa apolisi ( I G ) m’dziko muno waunikira kuti...
Imfa ya mphangala ya ndale a John Zenus Ungapake Tembo yaonetsa kuti Amalawi ndi amodzi ngakhale kusiyana kwa zipani za...
Mafumu apereka maganizo osiyanasiyana pa ganizo la boma lochotsa maina 1 miliyoni mu pulogalamu ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo...
Dziko la Malawi likugwiritsa ntchito pafupifupi K3 biliyoni pa chaka popereka thandizo kwa amayi amene anachotsa mimba pogwiritsa ntchito njira...
Abale a gogo Binwell Chabwera amene adathawitsidwa pomuganizira kuti adapha mdzukulu wake m’matsenga anenetsa kuti iwo sakufunanso kuona gogoyo. Gogo...
Bwalo la Nsanje Third Grade Magistrate lalamula amuna awiri kukagwira ukaidi kwa miyezi 24 atawapeza wolakwa pa mlandu woba mafoni....
Alimi ena amene afika ku chionetsero cha ulimi chimene nduna ya za malimidwe a Sam Kawale adatsegulira dzulo mu mzinda...
Pamene aphungu a Nyumba ya Malamulo amayembekezeka kukwangula zokambirana zawo dzulo, mkulu wa bungwe loona za ufulu wa anthu la...
Ng’anga ina ku Balaka yapereka chindapusa cha K90 000 kupewa kukaseweza miyezi 15 imene adamugamula atapezeka wolakwa pa mlandu woti...
Nduna ya za malimidwe a Sam Kawale ati kampani yogula mbewu ya Admarc siyitsegulidwa kuti iyambe kugula mbewu pokhapokha anthu...