Category: Chichewa

Muli mphamvu mu ukhondo

Bungwe la Water for People Malawi (WPM) lomwe cholinga chake n’kuonetsetsa kuti anthu m’dziko muno azimwa madzi aukhondo, komanso kukhala ndi zimbudzi zabwino lati…
Samalani maso popewa khungu

Khungu ndi amodzi mwa matenda a maso opeweka. Katswiri wa maso pa chipatala cha Chiradzlu Frank Mwamadi wati izi zimachitika munthu akasamalira bwino maso…
Ulimi wa njuchi ndi ofesi yonona

Kodi ulimi wa njuchi mudayamba liti? Ulimiwu ndidayamba mu 2017. Nanga chidakukopani n’chiyani? Nditalingalira mozama ndidaona kuti ulimi wa njuchi sulira zinthu zambiri monga…
DPP madzi afika mkhosi—Muntali

Zipani zotsutsa zati n’zodabwa kuti boma lagundika kukweza anthu ogwira ntchito m’boma, komanso kulipira mafumu nthawi ino ya kampeni pamene mmbuyo monsemu akhala akudandaula…
Mafumu atsegula  Njira ya kampeni

Pamene kampeni yafika pachiindeinde, zipani zandale zati n’zokhutira ndi momwe mafumu akuperekera mwayi wochititsa misonkhano yokopa anthu m’madera mwawo kwa zipani zotsutsa. Katswiri wa…
Apolisi adabwitsa chipani cha UTM

n’chodabwa ndi momwe apolisi, komanso a bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) akuyendetsera madandaulo awo. Mlembi wa chipanicho, Patricia Kaliati, adati adakatula dandaulo la…
Khama mu ulimi wa mtedza

Kwa alimi monga  Lipherani Mkhupera wa m’boma la Zomba, amachengetera bwino mbewu ya mtedza kuti apindule nayo.  Chifukwa cha ichi, ulimi wa mtedza ndi…

Akundidabwitsa Anatchereza, Ndili pa chibwenzi ndi mwamuna wina. Chomwe chimandidabwitsa n’choti nthawi zonse ndikamuimbira foni usiku samayankha. Ndikamufunsa amati idali kotchajitsa. Gogo ndikuona ngati…
Akuti akukumana  Ndi womwalira

Maloza! Mtembo wa mtsikana uli m’nyumba, manda atakumbidwa, anthu ena amakumana naye akungozungulirazungulira pamsika komanso m’munda mwa makolo ake. Anthu a m’mudzi mwa Mponda…
Lule adachita chokong’ontha

Lipoti la chipatala lomwe dotolo wotchuka pa zofufuzafufuza, Charles Dzamalala, watulutsa latsimikiza kuti woganiziridwa kusowetsa mwana wa chialubino, Buleya Lule adachita kuphedwa ndi shoko…
DPP ikutolera  Nambala zovotera

Ziyangoyango pa chisankho! Anthu ena achipani cha DPP akuti akutolera nambala za ziphaso za unzika, komanso zovotera kwa anthu amene adalembetsa. Izi zikuchitika ku…

Ndikufuna kuchoka Zikomo Anatchereza, Ndidabwera kutauni kudzafuna ntchito ndipo ndidasiya mkazi wanga kumudzi. Ntchito ndidaipeza koma abale amene ndimakhala m’nyumba yawo akuti ndisachoke kukafuna…
‘Ndidadabwa ndi dzina lake’

Dzina loti Mpunga lidadabwitsa njoleyo. Poti akatsimikize ngatidi dzinalo lidali la munthu, adakakumana ndi mbalume za bamboyo ndipo tikunenamu apangitsa chinkhoswe ukwati ulipo August…