Category: Chichewa

Manifesito ya UTM mulinji?

Akadaulo pa ndale ayamikira manifesito ya chipani cha UTM kuti ikuyankha mavuto amene dziko lino likukumana nawo komabe achenjeza chipanichi kulonjeza zokhazo zomwe akuganiza…

Adandichotsa ntchito Zikomo Gogo Ndakhala ndikugwira ntchito kwa bwana wina mumzinda wa Blantyre kwa zaka 4. Masiku apitawa ndidaapempha holide ya masiku 10 ndipo…
Mwana wa zaka 13, mavuto osakata

Ikakuona litsiro mvula siyikata. Mwambiwu wapherezera pa msungwana wina wa Sitandade 7 (yemwe sitimutchula dzina) pasukulu ina ku Chikwawa. Izi zidadziwika achipatala atamupeza msungwanayo…
Wa gulewamkulu atuluka pa belo

Bwalo la milandu m’boma la Kasungu lapereka belo kwa munthu yemwe adayerekeza kuvala gulewamkulu ndipo akuganiziridwa kuti adagwirira mwana wa zaka 7 pomwe mwanayu…
Tikolole motani chimanga?

Alimi m’madera a dziko lino amakolola chimanga mosiyanasiyana malingana ndi kuzolowera kwawo koma mphunzitsi wa kunthambi ya za maphunziro a za ulangizi ku Lilongwe…
Chenjerani pokolola

Mbewu ya chimanga nayo imafuna kuyichengetera nthawi yokolola kuti zokolola zikhale zochuluka ndi zopatsa kaso. Wachiwiri kwa mkulu woona za kafukufuku wa mbewu ku…
Kusakatula manifesito ya MCP

Loweruka pa 9 March chipani cha MCP chidakhala choyamba kukhazikitsa manifesito ake pokonzekera chisankho chapatatu chomwe chichitike pa May 21. Chipanicho chakhudza madera onse…
Ku Nsanje akukana zosamuka

“Ife zosamuka ayi,” yanenetsa gulupu Karonga ya kwa mfumu yaikulu Mlolo m’boma la Nsanje. Mawu a mfumuyo akudza pamene anthu 56 pofika Lachinayi sabata…
Aphungu akumana komaliza

Nthawi yatha. Aphungu a Nyumba ya Malamulo amene adasankhidwa mu 2014 akumana komaliza kuyambira Lachiwiri likudzali Amalawi asanavote pachisankho cha patatu pa 21 May…
Ras Chikomeni sizidamukomere

Pofika Lachisanu Ras Chikomeni Chirwa adali yakaliyakali kusakasaka K2 miliyoni kuti akapereke ku bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC). Izi zimadza pamene…