Chichewa
-
Samalani: Kwabuka matenda a chimanga
…Boma liletsa kugula mbewuyi m’maiko akunja okhudzidwa Chilinganizo cha boma choletsa kugula chimanga m’maiko a South Sudan, Uganda, Kenya, DR…
Read More » -
Ma Queens alephera ofikafika
Zowawitsa! Mpake Mwawi Kumwenda ndi Sindi Simtowe adalira ching’ang’adza Lachisanu atalephera pango’nong’ono kuwolotsa ma Queens kuti afike m’ndime ya…
Read More » -
Ntchito za Kumbu Kalipo (KK)
Tsikulo pa Wenela padaterera ndithu. Aliyense adali ndi chodzala tsaya chimwemwe. Sindikudziwa kuti zidali choncho chifukwa chiyani. Komatu ngakhale kudali…
Read More » -
Anatchezera
Banja lavuta Zikomo Anatchereza, Ndine mayi wa zaka 30 ndipo ndili ndi ana atatu. Kumbuyo kunseku timakhala bwinobwino ngakhale ndimamva…
Read More » -
‘Kudali kumapemphero’
Mawu a Mulungu amati: Kodi simudziwa kuti iwo akutumikira za m’kachisi amadya za m’kachisi… Mawu a Mulunguwa adakwaniritsidwa pomwe Rose…
Read More » -
Amangidwa kaamba kobisa khanda
Pamene amayi ena akukangana ndi amuna awo m’midzimu kufuna nsalu yalekaleka, amayi ena ndi pamene mwayi woterewu akumauseweretsa n’kumataya ana…
Read More » -
Amati aukitsa wakufa koma athera m’zingwe
Mudali fumbi m’mudzi mwa Mpheziwa kwa T/A Kasumbu m’boma la Dedza posachedwapa pamene khwimbi la anthu lidakhamukira m’mudzimo kukaonerera ntchito…
Read More » -
Kwagwedezeka ku PP
Potsata mawu a mtsogoleri wakale wa dziko lino Bakili Muluzi onena kuti chipani cha MCP “chatha ngati makatani”, zikuoneka kuti…
Read More » -
Sakumvanabe pa nkhani za ufumu
Pali kusamvanabe pakati pa unduna wa maboma aang’ono ndi mafumu a m’mizinda amene boma, kudzera mu undunawu, lidawalembera kalata yowadziwitsa…
Read More » -
‘Chikondi chidayambira kuubwana’
Akuti chikondi chidayambira kuumwana kalelo pomwe ankasewerera limodzi n’kumakula pa Kalera ku Salima ndipo lero akhala thupi limodzi. Francis Tayanjah-Phiri,…
Read More » -
Anatchereza
Amandimenya Anatchereza, Ndine mtsikana wa zaka 19 ndipo ndili ndi bwenzi la zaka 21 yemwe ndili naye mwana mmodzi. Dandaulo…
Read More » -
Amukwidzinga Pachinkhoswe
Amati mbuzi ikakondwa amalonda ali pafupi. N’zoonadi, Ili lidali tsiku lachisangalalo ndipo kudali kuvina, amayi nthungululu zili pakamwa. Anthu adabwera…
Read More » -
Ma Queens adyamo mu South Africa
Zatheka basi! Tikamati timu ya ntchemberembaye ya dziko lino ndi mizwanya mu Africa muno si tchetera, ayi. Izi zaoneka poyera…
Read More » -
Adona Hilida afika pa Wenela
Adafika pa Wenela tsikulo Abiti Patuma akuimba nyimbo yatsopano ya Lucius Banda. Inde ija waimba ndi Thocco Katimba: Mwandikumbuka. Yahwe,…
Read More » -
Mwangonde: Khansala wachinyamata
Akamati achinyamata ndi atsogoleri a mawa, ambiri amaganiza kuti izi ndi nkhambakamwa chabe. Koma achinyamata ena, monga Lusubilo Mwangonde,…
Read More » -
Apolisi alandira uphungu paziphuphu
Bungwe lolimbana ndi mchitidwe wa ziphuphu ndi katangale la Anti-Corruption Bureau (ACB) laphunzitsa apolisi a mumzinda wa Mzuzu za momwe…
Read More » -
Ntchito iyamba September uno
…Boma liyamba kuthandiza okhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi Boma lati ntchito yokonza zinthu zomwe zidawonongeka ndi chigumula cha madzi osefukira…
Read More » -
Mwambo wogwetsa simba
Sukulu zatsekera ndipo zikatere m’maboma ambiri makolo ali kalikiriki kukonzekera kuti ana awo apite kusimba kukavinidwa. Kumenekotu kumakhala uphungu kuti…
Read More » -
Pepani Ng’onamo, Chirwa
Kudali ntchito ku FAM pamene amafuna kochi wa timu ya fuko ya Flames. Eddie Ng’onamo, Nsanzurwimo Ramadhan, Ernest Mtawali…
Read More » -
Utsi ku Nam pamene ma Queens anyamuka
Utsi ukufukabe ku bungwe loyendetsa masewero a ntchemberembaye la Netball Association of Malawi (NAM) kaamba kosemphana zochita pakati pa mphunzitsi…
Read More »