Chichewa
-
Utsi ku Nam pamene ma Queens anyamuka
Utsi ukufukabe ku bungwe loyendetsa masewero a ntchemberembaye la Netball Association of Malawi (NAM) kaamba kosemphana zochita pakati pa mphunzitsi…
Read More » -
Mkulu wa zaka 22 akaseweza zaka 23
Wakhala akuthyola nyumba masana kasanu konse ndi kubamo katundu. Anthu ku Balaka akhala akumusaka koma adali woterera ngati mlamba. Koma…
Read More » -
Zavutanso ku Mozambique
Othawa nkhondo ayamba kufika m’dziko muno Zavutanso ku Mozambique. Nkhondo ya pachiweniweni pakati pa otsatira chipani cholamula cha Frelimo ndi…
Read More » -
Yamikani ‘Headmaster’ Fodya wa Bullets
Dzina la Yamikani Fodya lawanda. Uyutu ndi mnyamata wokankha chikopa kutimu ya Flames komanso ku Big Bullets. Iyeyu wapatsidwa maina…
Read More » -
Anatchezera
Wamboni, ine Msilamu Zikomo Anatchereza, Ndinagwa m’chikondi ndi mtsikana wa Mboni za Yehova mpaka ndinamuchimwitsa moti ndikunena pano kuli mwana…
Read More » -
A khonsolo ndi ankhanza—Amalonda
Ena mwa ochita malonda (mavenda) m’misewu ya mumzinda wa Blantyre alira ndi khalidwe la akhonsolo ya mzindawu kuti akuwachitira nkhanza…
Read More » -
‘Tidali maneba ku Gulliver’
Mawu akuti mbuzi imadya pomwe aimangilira amamveka achabe koma nthawi zina mawuomwewa amakhala ndi tanthauzo lopambana, maka potengera zipatso zomwe…
Read More » -
Mayi wamalonda avulazidwa ku bt
Titha Masamba, wa zaka 31, akumva ululu wadzaoneni. Kuti ayende akuyenera agwirire ndodo; sangagone chafufumimba koma chammbali kapena chagada; moyo…
Read More » -
Njoka zoweta ndi penshoni
Pa Wenela tsikulo padafika ng’anga ina imene inkati yangofika kumene kuchokera ku Mozambique, inde dziko la nkhondo. Ng’angayo idafika ndi…
Read More » -
Ulimi wa tomato, kabichi ndi nyemba wakolera
Alimi abebetsa ulimi wa tomato, kabitchi komanso nyemba m’boma la Ntcheu pamene ulimi wa m’madimba wachiwiri wayambika. Boma la Ntcheu,…
Read More » -
‘Ulimi wa fodya usafe’
Maiko asanu ndi awiri a kummawa ndi kummwera kwa Africa agwirizana zogwirira ntchito limodzi pofuna kutukula ulimi wa fodya womwe…
Read More » -
Mantha pa Wenela
Titakhala pamalo aja timakonda pa Wenela, adafika gogo wina. Iye adavala nkhope yachisoni. “Ana inu, mwataya chikhalidwe. Mwalowerera kuba, kupha…
Read More » -
KWAVUTA KUMSIKA WA NKHOTAKOTA
Kunjatidwa kwa mkulu wina m’boma la Nkhotakota kwavumbulutsa nkhani yosalana mumsika wa m’bomali. Woyendetsa ntchito za polisi ya m’bomali, Station…
Read More » -
Zig Zero: Mnyamata wa nyimbo za dansi
Kuyambira kuubwana wake chimene amaganiza, kulota ndi kuchita ndi kuimba nyimbo basi. Inde, Mulungu adamudalitsa ndi liwu lanthetemya mnyamata ameneyu…
Read More » -
‘General Kanene’ watuluka m’ndende
Mtsogoleri wa dziko la Zambia Edgar Lungu wakhululukira ndi kulutsa mundende General Kanene, woimba wotchuka m’dzikolo, yemwe dzina lake lenileni…
Read More » -
‘Jersey No. 8 ndiyo idandigwetsa m’chikondi’
Olemba, lembani. Veronica Mukhuna lero wasintha dzina ndipo ndi Veronica Zakazaka. Za mpira zenizeni, pamene Gomezgani Zakazaka, woyendetsa za mipikisano…
Read More » -
ANATCHEZERA
Sitinakumanepo Anatchereza, Ine dangwa m’chikondi ndi munthu woti sindinakumanepo naye. Ndili ndi zaka 23 koma iye ndikamufunsa zaka zake samandiuza.…
Read More » -
‘Amayi akhale odzidalira’
Mkulu wa bungwe la Beautify Malawi Trust (Beam Trust), Gertrude Mutharika, walimbikitsa amayi m’dziko muno kuti akhale odzidalira pachuma. Mutharika…
Read More » -
Atenge ligi yaTNM ndani?
Akatswiri pa zamasewero ndiye akamba, aphunzitsi nawo ndi ochemerera alosera zambiri koma kamuna adziwika lero nthawi ikamati 4:00 madzulo ano.…
Read More » -
PAC iunguza za boma la ‘chifedulo’
Nthumwi zomwe zimakumana mumzinda wa Blantyre kukambirana za nkhani yakuti zigawo za dziko lino zizikhala ndi mtsogoleri wakewake pansi pa…
Read More »