Category: Chichewa

Ma MP olowa PP akonzekere nkhondo

Mphunzitsi wa zandale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College (Chanco), komanso anthu ena ati chipani cholamula cha People’s (PP) chikuyenera kusamala malamulo potolera anthu…

Amalawi m’zigawo zonse m’dziko muno apereka ulemu wawo wotsiriza kwa yemwe adali mtsogoleri wa dziko lino, Bingu wa Mutharika.

Mafumu, mphunzitsi wandale kusukulu ya ukachenjede ku Chancellor College kudzanso Amalawi ena ati mchitidwe wa andale ena posintha zipani kuti alowe chipani cholamula—chonsecho maliro…

Chisangalalo chadzanso kwa Achewa a m’boma la Mwanza pomwe T/A Kanduku wa m’bomalo walengeza Lolemba pa 26 Malitchi kuti madambwe onse omwe adawatseka atsekulidwenso.

Anthu m’midzi ingapo m’boma la Mwanza akunyanyala ntchito zachitukuko pokwiya ndi ganizo la mfumu yayikulu T/A Kanduku loti Achewa m’dera lake ayambe kutsatira Chingoni.
Mafumu akhumudwa ndi kuvula amayi

Mafumu komanso anthu m’dziko muno ati ndiokhumudwa ndi zomwe oganiziridwa kuti ndi mavenda m’mizinda wa Lilongwe, Blantyre ndi Mzuzu m’sabatayi povula mbulanda amayi omwe…

Mavenda 40 omwe adamangidwa mu mzinda wa Lilongwe sabata yathayi ali m’gulu la anthu zikwizikwi za anthu amene akhudzidwa ndi kunyanyala ntchito kwa anthu…