Category: Chichewa

Ma MP olowa PP akonzekere nkhondo

Mphunzitsi wa zandale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College (Chanco), komanso anthu ena ati chipani cholamula cha People’s (PP) chikuyenera kusamala malamulo potolera anthu…

Amalawi m’zigawo zonse m’dziko muno apereka ulemu wawo wotsiriza kwa yemwe adali mtsogoleri wa dziko lino, Bingu wa Mutharika.

Mafumu, mphunzitsi wandale kusukulu ya ukachenjede ku Chancellor College kudzanso Amalawi ena ati mchitidwe wa andale ena posintha zipani kuti alowe chipani cholamula—chonsecho maliro…

Chisangalalo chadzanso kwa Achewa a m’boma la Mwanza pomwe T/A Kanduku wa m’bomalo walengeza Lolemba pa 26 Malitchi kuti madambwe onse omwe adawatseka atsekulidwenso.
‘Boma lalowa nthenya’

Mphunzitsi kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, Blessings Chinsinga, wati kumangidwamangidwa kwa anthu omwe akuoneka kuti siabwenzi a boma kukutanthauza kuti boma la DPP…

Anthu m’midzi ingapo m’boma la Mwanza akunyanyala ntchito zachitukuko pokwiya ndi ganizo la mfumu yayikulu T/A Kanduku loti Achewa m’dera lake ayambe kutsatira Chingoni.
Mafumu akhumudwa ndi kuvula amayi

Mafumu komanso anthu m’dziko muno ati ndiokhumudwa ndi zomwe oganiziridwa kuti ndi mavenda m’mizinda wa Lilongwe, Blantyre ndi Mzuzu m’sabatayi povula mbulanda amayi omwe…