Chichewa
-
Akhazikitsa ntchito yolimbana ndi Edzi
Boma mogwirizana ndi bungwe la Elizabeth Glaser Pediatric Aids Foundation ati ndondomeko yatsopano yolimbana ndi matenda a Edzi ya ndalama…
Read More » -
Miyezi inayi idutsa mafumu osalandira mswahala
Nyakwawa komanso magulupu akudandaula kuti matumba awo abooka kaamba koti patha miyezi inayi asakulandira mswahala. T/A Nthache wa ku Mwanza…
Read More » -
Mtsutso pa za makanda odabwitsa
Mtsutso wakula ngati n’koyenera kuti ana obadwa modabwitsa azituluka m’chikuta. Izi zadza mwana wina wankhope yodabwitsa atabadwa kuchipatala cha Salima…
Read More » -
Akuti zipolowe zichepe
Zipolowe kaamba ka ndale zomwe zakhala zikuchitika m’dziko muno zikupereka chiopsezo kuchisankho cha chaka chamawa komanso kutekesa mtendere wa dziko…
Read More » -
‘JB watukula amayi, koma ntchito ikadali’
Pamene dziko la Malawi lagwirana manja ndi maiko ena padziko lapansi pokukumbukira tsiku la amayi, Amalawi ena athirapo ndemanga ndi…
Read More » -
Zipolowe atamangidwa Mutharika
Kumangidwa kwa anthu 11 omwe akukhudzidwa ndi nkhani yofuna kulanda boma Bingu wa Mutharika atamwalira sikudakomere anthu ena amene adachita…
Read More » -
Lipoti la imfa ya Bingu latekesa boma, DPP
Pomwe Malawi waona utsi wokhetsa misozi chifukwa cha kumangidwa kwa mamulumuzana a DPP komanso amaudindo ena m’boma, akadaulo pazandale komanso…
Read More » -
Ndalama zakale zitha pa 23 May
Banki yaikulu yakumbutsa mabanki a m’dziko muno kuti ndalama zakale za ‘Chilembwe’ dziko lino zisiya kugwira ntchito pa 22 May.…
Read More » -
‘Chibaluwa chasiya zina’
Pamene kwangotha sabata mpingo wa katolika utatulutsa chikalata chounikira momwe zinthu zikuyendera m’dziko muno, katswiri wa ndale kusukulu ya ukachenjede…
Read More » -
Akulimbana ndi Edzi
Pothandiza kuti uthenga wokhudza matenda a EDZI ufikire achinyamata ambiri makamaka pobweretsa uthengawo pafupi ndiponso kunjira zomwe achinyamata akugwiritsa ntchito…
Read More » -
Gawo 65 lavuta
DPP inenetsa sipikala achotse aphungu ochoka chipani Chipani cha DPP chati sichilola kuti nkhani yokhudza Sekishoni 65 yomwe imapatsa mphamvu…
Read More » -
Sitalaka yatha, yaika amalawi pamoto
Pomwe ogwira ntchito m’boma ali pa sitalaka kufuna kuti malipiro awo akwere ndi K67 pa K100 iliyonse, anthu omwe amafuna…
Read More » -
‘Mawu a JB ndi loto’
Akuluakulu a mabungwe ena ati mawu a mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda potsegulira msonkhano wa aphungu Lachisanu lapitalo ndi…
Read More » -
‘Ngakhale odulidwa kale adulidwe’
Amuna amene adadulidwa potsatira chipembedzo kapena chikhalidwe ayenera kudulidwanso, ngati sanadulidwe moyenera, watero mkulu woona za ntchito ya mdulidwe muunduna…
Read More » -
Mulanje yadya wani pa chitukuko
Boma la Mulanje ladya wani pogwiritsa ntchito ndalama za thumba la chitukuko m’dera la phungu la Constistuency Development Fund (CDF),…
Read More » -
Chimanga kulibe amalawi adandaula ndi Admarc
Pamene njala ikupitirira kukantha m’madera ena, zadziwikanso kuti m’misika ya Admarc yambiri m’dziko muno mulibe chimanga ndipo anthu ku Ntcheu,…
Read More » -
Kwaipa ku chipatala, mankhwala atha
Mwa mankhwala 100 amene amayenera kupezeka m’zipatala za boma, asanu okha ndiwo alipo, Nduna ya Zaumoyo Catherine Gotani-Hara idatero ku…
Read More » -
Aphungu apane boma posakaza chuma
Pamene aphungu a ku Nyumba ya Malamulo ayambe kukumana pa 8, mkulu wa bungwe loona zachilungamo pachuma la Malawi Economics…
Read More » -
MCP ichotsa anthu 30
Chipani cha MCP chachotsa mamembala 30 a chipanichi ku Mzuzu powakaikira kuti amagwirizana ndi mlembi wamkulu wa chipanichi Chris Daza.…
Read More » -
Boma liunikire mfundo zotsatira zionetsero
Kuyankha mfundo 7 zimene anthu adapereka pakutha pa zionetsero zosonyeza kukwiya kwa Amalawi ena ndi mfundo zina za chuma m’boma…
Read More »