Chichewa
-
Mafumu ayamikira kuyamba kwa ziphaso
Mafumu m’dziko muno ati kuyamba kwa ntchito yopanga ndi kupereka ziphaso zosonyeza unzika, ndi chiyambi chopititsa patsogolo ntchito za chitukuko…
Read More » -
Amabungwe akukonzanso zogwirira ntchito limodzi
Pozindikira kuti mutu umodzi susenza denga, mabungwe omwe si aboma omwe akugwira ntchito zosiyanasiyana m’dziko muno, kuphatikizapo za maufulu a…
Read More » -
Kumawachenjeza anawa
Ndimakumbuka kuti masiku adzanawo, nkhani zogwiririra anazi zisanafale kwenikweni, mayi wanga ankatikhazika pansi, ine ndi achemwali anga, kutiuza kuti…
Read More » -
Mwambo wa ukwati wa Chitonga
Mtundu wina uliwonse uli ndi chikhalidwe chake. Ndipo nawo mtundu wa Atonga womwe umapezeka kwambiri ku Nkhata Bay ndi…
Read More » -
Mitsinje isefukiranso chaka chino—azanyengo
Nthambi yopima zanyengo ya mdziko muno ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati chaka chino kukhala kusefukira…
Read More » -
Osiyidwa pachilumba cha Ruo alira koto!
Ndi 5 koloko mmawa, Belita Zakeyu wa m’mudzi mwa Manthenga kwa T/A Mlolo m’boma la Nsanje wafika kale m’manda a…
Read More » -
A Escom adziwe kuti takwiya—Kapito
Si zachilendonso, nyimbo yomwe aliyense akuimba ndi kuzimazima kwa magetsi. Mmalo mopereka magetsi tsiku lililonse monga anenera, ayamba kupereka mdima…
Read More » -
Kuthimathima kwa magetsi kwakhudzanso akumidzi
Ndi Lolemba mmbandakucha wa pa 12 September, nthawi yangokwana kumene 4 koloko koma magetsi azima kale m’boma la Mulanje. Chiyembekezo…
Read More » -
Gulewamkulu ndi mankhwala
Matenda akagwa pakhomo, makolo amakhala ndi njira zochuluka zothetsera matendawo malinga ndi zikhulupiriro zawo. Ena okhulupirira gulewamkulu akuti ngati m’thupi…
Read More » -
Msonda: Tsamba loyoyoka mu PP?
Nthawi yomwe anthu akuchoka m’chipani cha Peoples Party (PP) chitangogwa m’boma, mneneri wa chipanichi, Ken Msonda, yemwe ali ndi lilime…
Read More » -
Siteshoni ya Nkaya ifewetsa maulendo
Gawo lachiwiri lomanga siteshoni ya sitima ya Nkaya m’boma la Balaka layamba ndipo ntchitoyi ikuyembekezeka kutha mu November chaka chino.…
Read More » -
TUM imemeza sitalaka ya aphunzitsi lolemba
…Makolo, katswiri apempha boma lichitepo kanthu Sukulu za boma za pulayimale ndi sekondale m’dziko muno zikuyembekezereka kuima kuyambira mkucha Lolemba…
Read More » -
Obera malova akuchuluka
Akapsala obera achimata amapepala awo powalonjeza ntchito zomwe chikhalirecho palibepo akuchulukirabe m’mizinda ngakhale kuti apolisi ndi unduna wa zantchito akulimbana…
Read More » -
Akwiya ndi bungwe la MEC
Mpungwepungwe umene ukuchitika kubungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) wakwiyitsa zipani zotsutsa komanso omenyera ufulu omwe apempha kuti…
Read More » -
MEC igwira njakata pa zisankho zapadera
Zinthu sizikuyenda kubungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) komwe tsogolo la zisankho zapadera silikudziwika. Lachitatu lapitali, mkulu wa…
Read More » -
Tinkakhala nyumba zoyandikana’
Mwayi wa banja umapezeka malo osiyanasiyana. Ena amapeza womanga naye banja mubasi, eetu paulendo, pomwe ena amakumana kutchalitchi. Koma…
Read More » -
Chu uyu mpaka liti?
Njala yayamba kuluma m’madera ena koma ngakhale zili chonchi, boma lati anthu asayembekezere kuti misika ya Admarc itsegulidwa msanga…
Read More » -
Dzombe kukoma, koma…
Kuyambira makedzana, panthawi ya ulendo wa ana Aisiraele kuchoka ku Aigupto kupita kudziko lolonjezedwa lija la Kenani ngakhalenso nthawi…
Read More » -
‘Luso la mpira ndilo lidandidolola’
Sabata zitatu zapitazo Sindi Simtowe adamanga ukwati ndi Ardron Msowoya, mnyamata yemwe akugwira ntchito ku Inde Bank. Kwa iwo amene…
Read More » -
Akana ‘nyau’ yogwiririra
Senior Chief Lukwa, mmodzi mwa mafumu akuluakulu a Achewa m’dziko muno, yemwenso amayankha pankhani za mafumu, wati munthu yemwe khothi…
Read More »