KCH seeks tutors for  child cancer patients

Kamuzu Central Hospital (KCH) has appealed to stakeholders to mobilise volunteers to teach children undergoing cancer treatment as they miss out on school due to long hospital stay. Global Hope programmes manager Mphatso Magwaya, whose organisation manages all programmes of paediatric cancer ward at KCH, said this when Lions Club of Bwaila prepared lunch for…

Nyumba ya Malamulo yakhutira ndi MEC

Komiti yolondoloza malonjezo a boma ku Nyumba ya Malamulo yati ndiyokhutira ndi lipoti la bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC). Bungwe la MEC lidawonekera pamaso pa komitiyo Lachiwiri m’sabatayi kukapereka lipoti la momwe zokonzekera za chisankho chapatatu zikuyendera. Polankhula ndi Tamvani, wapampando wa komitiyo Yaumi Aufi Mpaweni adati lipoti la MEC likusonyeza kuti…

Kupereka makalata ofuna kudzaimira m’chisankho chikudzachi ndiye kwatha, maso tsopano ali pazomwe zipani zasanja kufuna kutukula dziko lino. Kuunguza kwa Tamvani kwapeza kuti mfundo zomwe zipani zasanja sizikusiyana kwambiri. Zipani za UTM, MCP ndi PP atsindika nkhani ya ntchito, ulimi, maphunziro ndi magetsi. Chipani cholamula cha DPP chakana kuulula manifesito ake ati chifukwa nthawi ya…

William Murray alumni renovate school’s toilets

William Murray Secondary School (Wimuss) Alumni Association in Lilongwe have renovated the school’s plumbing system which had been faulty for years. The group’s chairperson Apostle Helix Jaxon Chigonammalunje said the former students discovered the school’s challenges following an assessment which was influenced by the school’s dwindling performance. “We observed that the school’s performance was going…

CMST iyambanso kugawa mankhwala

Nkhokwe ya mankhwala ya Central Medical Stores Trust (CMST) yatsiriza kukambirana ndi mabungwe omwe amathandiza dziko lino pa nkhani ya zaumoyo kuti udindo wosunga ndi kugawa mankhwala ubwerere m’manja mwake. Mkulu woyendetsa ntchito zaumoyo m’dziko muno, Dr Charles Mwansambo, komanso mkulu wa CMST, Feston Kaupa, atsimikiza za nkhaniyi. Akuluakulu awiriwa ati izi zikutanthauza kuti mabungwe…

UNFPA for youth empowerment

United Nations Population Fund (UNFPA) country representative Young Hong says youths need to be empowered to make informed decisions on their reproductive health. Speaking on Thursday during the launch of the 2018 State of the World Population Report at Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar), Hong said the youth need to take the…

MEC yachotsa maina 13 244 m’kaundula

Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) lachotsa m’kaundula maina 13 244 omwe eni ake adawalembetsa kopotsera kamodzi zomwe lati n’zotsutsana ndi malamulo azitsankho. Wapampando wa bungweli Jane Ansah ndiye adalengeza izi Lachiwiri mu mzinda wa Lilongwe moti eni mainawo azengedwa mlandu wophwanya malamulo azisankho a dziko lino. “Maina ena amapezeka kangapo m’kaundula ndiye tawachotsa koma…

Project reveals gender violence in colleges

EngenderHealth Malawi,through its Essential Gender-Based Violence (GBV) Prevention and Servicesproject, has said female students in various colleges experience genderviolence. EngenderHealth Malawi’s project director Chisomo Kaufulu-Kumwenda said this during a sensitisation campaign for first year students at Bunda College of Agriculture, a constituent college of the Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar), on Thursday…

Malawi gets K18.5bn for GBV fight

  The European Union (EU) has given Malawi 22 million euros (about K18.5 billion) for programmes aimed at ending violence against women and children. United Nations Development Programme (UNDP) portfolio manager responsible for Institutions and Citizen Engagement Agnes Chimbiri, said EU is working with the United Nations (UN) in the programme. She said: “The programme…

Kafukufuku wa chamba watha

Zotsatira za kafukufuku wa ulimi wa chamba zomwe Amalawi akhala akudikira zatuluka koma mlembi wa unduna wa zamalimidwe, mthilira ndi chitukuko cha madzi Gray Nyandule Phiri wati zotsatirazi akuzisunga mwachisinsi. Phiri wati zotsatirazi zomwe kafukufuku wake watha zaka zitatu ziyamba zapita ku ofesi ya presidenti ndi nduna zake (OPC) kuti akaziunike zisadaulutsidwe kwa Amalawi. “Kafukufukuyu…

High Visa fees chocking tourism

The tourism sector in the country is failing to reach its full potential due to challenges such as high VISA fees and lack of competition in the aviation industry, Malawi Tourism Council (MTC) has said. MTC board chairperson Oswald Bwemba said during the tourism stakeholders conference in Salima on Thursday that with the VISA fees…