Chichewa
-
Alendo alanda maudindo mu PP
Kusankhidwa kwa ‘alendo’ ochoka m’zipani zina kukhala m’maudindo onona kuchipani cholamula cha People’s (PP) kungakolezere mavuto kuchipaniko, maka pandawala yolowera…
Read More » -
Kudziwa za m’thupi; kukonza tsogolo
Sabata yatha inapatulidwa ndi boma pankhani yoyezetsa magazi kuti anthu adziwe ngati ali ndi kachirombo koyambitsa Edzi ka HIV. Mutu…
Read More » -
Akufuna wogwirizira ufumu achoke, apepese
Mafumu m’dziko muno agwirizana ndi ganizo la mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda kuti magulupu ndi nyakwawa asiye kulandirira ndalama…
Read More » -
Moto wayaka ku Nkosini
Pasanadutse n’komwe mwezi chilongere Inkosi Yamakosi Gomani Yachisanu ku Ntcheu, fumbi labuka pomwe mbali ina kubanjalo ikukakamiza wogwirizira, Rosemary Malinki…
Read More » -
Moto utentha misika, njakata izinga
A malonda omwe katundu wawo adapsera m’misika ya mavenda ya Tsoka ku Lilongwe komanso wa Blantyre akulira chokweza, uku akupempha…
Read More » -
Mswati akhale chitsanzo kwa achinyamata
Pulezidenti Joyce Banda wati mfumu yachingoni yomwe angoidzoza kumene, Mswati Kanjedza Gomani yachisanu ikhale chitsanzo kwa achinyamata. Banda amalankhula izi…
Read More » -
Kuyezetsa magazi kwayenda bwino
Mlembi wamkulu mu Unduna wa Zaumoyo wati sabata yolimbikitsa kuyezetsa magazi pofuna kudziwa ngati uli ndi kachilombo koyambitsa Edzi idali…
Read More » -
Akufuna lamulo lothana ndi uchidakwa
Unduna wa zaumoyo wati ukukonza lamulo lomwe cholinga chake n’kulonderapo pa kamwedwe kamowa m’dziko muno. Woyang’anira za matenda osapatsirana muundunawu…
Read More » -
Amalawi akulira, chitetezo chachepa
Akuluakulu a mabungwe omwe siaboma ati kuchepa kwa malipiro a apolisi ndi chimodzi mwa zomwe zalowetsa pansi chitetezo m’dziko muno…
Read More » -
Achotsa mavenda popanda ziwawa ku Lilongwe
Kunali njinga yapulula machaka ku Lilongwe Lachisanu lapitalo pomwe anthu mazanamazana amabwerera m’makwawo opanda kanthu m’manja atalephera kukolola posalima akuluakulu…
Read More » -
DPP idzudzula boma
Chipani chakale cholamula cha Democratic Progressive (DPP) chati Amalawi angapitirire kusauka ngati boma la chipani cha People’s (PP) silibwera msanga…
Read More » -
Kusanthula ulamuliro m’masiku 100 a Banda
Boma la mtsogoleri wa dziko lino, Joyce Banda, likuyenera kukhwimitsa chitetezo m’dziko muno, kuchepetsa kumanga anthu chisawawa komanso kuchepetsa kuchotsa…
Read More » -
Chitetezo chachepa, tithandizeni—anthu
Anthu m’dziko muno apempha boma kuti lichite changu pobwezeretsa chitetezo chomwe ati chalowa libolonje m’masiku apitawa. Izi zalankhulidwa m’kati mwa…
Read More » -
Gawo 65 yazunguzanso mitu aphungu
Mpungwepungwe wabukanso ku Nyumba ya Malamulo pomwe pali kuponyerana Chichewa pakati pa aphungu achipani cha DPP ndi aphungu omwe adachoka…
Read More » -
‘Bingu adafa bwanji, pakhale kafukufuku’
A mabungwe omwe si a boma, mfumu ina yaikulu komanso anthu angapo otumikiridwa ati n’koyenera kuti Amalawi adziwe bwino lomwe…
Read More » -
Malawi siidalakwe za al-Bashir
Mphunzitsi wa za mbiri yakale ku sukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, Pulofesa Chijere Chirwa wati dziko lino silingakhudzidwe m’njira…
Read More » -
‘Bajeti sidaganizire anthu akumudzi’
 Ali ndi mwana agwiritse, akutero amabungwe ati poti ndondomeko ya boma ya chuma ya chaka cha 2012 mpaka 2013…
Read More » -
UDF ingaphe demokalase
Zomwe achita aphungu a chipani cha UDF pokapezeka mbali ya boma m’Nyumba ya Malamulo zingaphe demokalase, watero mphunzitsi wa zandale…
Read More » -
Anthu 50 000 akutenga HIV chaka chilichonse
Pamene nkhondo yolimbana ndi matenda a Edzi ikupitirira, zadziwika kuti chaka chilichonse anthu 50 000 akutenga kachirombo ka HIV kamene…
Read More » -
Kwacha yagwa, valani zilimbe
Anthu akumudzi ati boma lifulumire kuika njira zowatchinjirizira ku zomwe zingadze kaamba ka kugwa kwa ndalama ya kwacha. Anthuwa ati…
Read More »