Chichewa
-
Amayi adandaulira boma ndi za HIV, Edzi
Bungwe la mgwirizano wa achipembedzo, zipani zandale komanso mabungwe omwe siaboma la Public Affairs Committee (PAC), layamba kuunikanso momwe Gawo…
Read More » -
UDF isankha Atupele akhale tcheya
Pomwe chipani cha UDF chikusangalala kuti chachititsa msonkhano waukulu omwe ati udali wokomera anthu, katswiri pandale, Joseph Chunga komanso mulumuzana…
Read More » -
Amayi adandaulira boma pa za HIV, edzi
Amayi omwe ali ndi kachilombo ka HIV koyambitsa matenda a edzi apempha boma kuti likonze zina mwa mfundo zake zoyendetsera…
Read More » -
Zokhoma pa makuponi
Ndondomeko ya fetereza wotsika mtengo [wa makuponi] chaka chino m’madera ena monga Dedza, Karonga, Zomba komanso Kasungu yatsimikizika kuti magulupu…
Read More » -
Ophunzira apewe uchidakwa—Polisi
 A polisi m’dziko muno achenjeza ophunzira kuti asiye uchidakwa popeza mchitidwewu ukuononga tsogolo lawo. Wachiwiri kwa mkulu woona ubale wa…
Read More » -
Njala yavuta, mafumu achenjeza
Mafumu ena m’dziko muno apempha boma kuti liwathandize kuthana ndi njala yomwe yayamba kale kusautsa maboma angapo ndipo madera ena…
Read More » -
JB wati mafumu alandira fetereza padera
Mafumu angapo ati alibe vuto ndi chilinganizo chatsopano cha Pulezienti Mayi Joyce Banda choti atsogoleriwa asalandire makuponi a panyumba pawo…
Read More » -
DPP igwa pa chisankho ku Mzimba
Katswiri pa ndale, mkulu womenyera ufulu wachibadwidwe, komanso anthu ku Mzimba ati kumbwita kwa chipani cha DPP pamasankho achibwereza ku…
Read More » -
Mabungwe apereke nzeru pamkangano wa nyanja
Kadaulo wa mbiri yakale, Kings Phiri, wati ndibwino dziko lino lipemphe bungwe la umodzi wa maiko a mu Africa la…
Read More » -
Ndale zikuwononga ufumu
Mafumu angapo ati zipani zolamula zimaononga mbiri ndi ntchito ya mafumu powakweza popanda kuyang’anira mbiri ya ufumuwo komanso khalidwe la…
Read More » -
Abusa chepetsani tsankho
Ngakhale ambiri amati padziko lapansi palibe chilungamo, anthufe timayembekeza kuti kumpingo kokha tikapezako kachilungamo popeza uku ndi kumene ambiri timaphunzirako…
Read More » -
Thalaveni isanduka powerengera mabuku
Anthu omwe amapita kukaziziritsa kukhosi ndi mowa wa Chibuku ku Zingwangwa mumzinda wa Blantyre ayiwale pomwe kampani ya Chibuku Products…
Read More » -
Akugulitsa magazi ku Mangochi
Kaamba ka kusowa magazi pachipatala cha Mangochi, anthu ena ozungulira chipatalacho akugulitsa magazi awo kwa odwala osoweka mwazi pamtengo wa…
Read More » -
Amalawi ati boma la PP likusakaza chuma
Akuluakulu ena ati boma la chipani cha People’s Party (PP) motsogozedwa ndi mtsogoleri wake, Joyce Banda kudzanso wachiwiri wake, Khumbo…
Read More » -
Chitetezo chibwerera m’chimake
Mkulu wapolisi m’dziko muno Lot Dzonzi wati uchifwamba omwe anthu ambiri akudandaula kuti wafika povuta tsopano utha chifukwa cha njira…
Read More » -
Kachali apepesa: Kulankhula motumbwa kuthe
Anthu, a mabungwe omwe siaboma, katswiri pandale kudzanso mfumu ina ati andale asamaledzere ndi maudindo n’kufika poiwala kulemekeza anthu omwe…
Read More » -
Nigeria, Malawi agwilana manja
Pamene dziko la Malawi lili mkati mwazokambirana ndi dziko la Tanzania pa nkhani ya umwini wa nyanja ya Malawi yomwe…
Read More » -
Amalawi akulira ndi kukwera kwa mafuta
Mkulu wa bungwe loona za ufulu wa ogula malonda la Consumers Association of Malawi (CAMA), John Kapito, wati boma lichite…
Read More » -
‘Kusowa kwa mpikisano n’kwachabe’
Pali mantha kuti zipani za m’dziko muno zingayoyoke ngati makatani ngati mipando yonona yachipani monga wa pulezidenti ndi wachiwiri wake…
Read More » -
Alendo alanda maudindo mu PP
Kusankhidwa kwa ‘alendo’ ochoka m’zipani zina kukhala m’maudindo onona kuchipani cholamula cha People’s (PP) kungakolezere mavuto kuchipaniko, maka pandawala yolowera…
Read More »