‘Tataya nanu chikhulupiriro’

Kwayaka moto! Zipani zina zotsutsa zati zilibenso chikhulupiriro ndi mkulu wa bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane Ansah ndipo amupempha kuti achoke. Izi zimalankhulidwa ku msonkhano wa National Elections Consultative Forum (Necof) womwe udachitikira ku Lilongwe Lachitatu m’sabatayi kutsatira mpungwepungwe womwe wabuka ku MEC. Msonkhanowo umachitika kutsatira kusowa kwa makina amene MEC…

Korean NGO for improved ECD

  The Lighthouse Foundation (LHF), a Korean non-governmental organization (NGO) says it is working on improving the capacity of child care givers in Traditional Authority (TA) Chigaru in Blantyre. The NGO organized a two-week training for 30 caregivers in conjunction with Association of Early Childhood Development in Malawi (AECDM) focusing on helping the caregivers to…

Rescued from jaws of resistant TB

Esther Loleya is the epitome of discrimination that comes with TB. She was chased from her marital home. Why? Her in-laws felt she would pass her multi-drug resistant TB to her husband. Bobby Kabango has followed her. He writes: It was a hot Tuesday, May 22 this year, when I first met her. Esther Loleya,…

Pasuwa starts with a win

  Nyasa Big Bullets new Zimbabwean coach Callisto Pasuwa yesterday made a winning start to his two and a half months stint after beating Dwangwa United 2-0 in a TNM Super League match at Kamuzu Stadium in Blantyre. However, it was strikers trainer Heston Munthali who still appeared to be in control as he barked…

Akulipitsa kulembetsa khadi

Anthu ena amene sadalembetse nambala zawo akulirira kuutsi pamene ma agenti ena akuwauza kuti alipire ngati akufuna nambala yawo ilembetsedwe. Izi zikudza pamene makampani a foni za m’manja a Airtel ndi TNM adachotsa nambala zimene sizidalembetse pofika pa 30 September chaka chino. Ngakhale kampanizi zidachotsa nambala zina, eni nambalawo ali ndi mwayi wokalembetsa nthawi iliyonse…

Angwanjula osalembetsa

Ngati mukuyesera kuimba foni koma sizikutheka, kapena mayunitsi sakulowa, ingodziwani kuti nambala yanu sidalembetsedwe ndipo ayithothola. Izi ndi zomwe anthu ena maka amene amagwiritsira ntchito netiweki ya TNM akumana nazo kucha kwa pa 1 October. Pamene ogwiritsira ntchito Airtel adaonanso mbonaona Lachitatu. Izi zikutsatira ganizo la boma lodzera ku bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority…

Kulumana pa ofunika kulandira chakudya

Kusankha ovutikitsitsa kuti alandire thandizo la chakudya kuchokera ku boma kwavuta m’midzi ina pamene anthu ndi mafumu ayamba kulumana. Izitu zadza pamene boma kudzera m’nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya Department of Disaster Management Affairs (Dodma) yayamba kugawa chakudya kwa anthu amene sadakolole chakudya chokwanira chifukwa cha ntchemberezandonda ndi ng’amba. Nthambi ya Dodma idapempha…

More rot at escom

Escom has been offering contracts to companies not registered with the Registrar General and avoiding clearance from the Public Procurement and Disposal of Assets Authority (PPDA) by “splitting” procurement deals, Nation on Sunday reveals. The revelations come on the heels of a series of  scandals that have rocked the parastatal, including a theft of 4.2…

Kusamvana pa zochotsa fizi

Ganizo la boma lochotsa fizi pa maphunziro m’sukulu za sekondale ladzetsa chisokonezo m’sukulu zaboma zina pomwe ophunzira ena akukana kulipira fizi ponena kuti boma lachotsa fizi. Sabata zitatu zapitazo, boma lidalangiza mahedimasitala kuti asatolere ndalama za sukulu fizi, yomwe ndi K500. Ndipo Lachwiri, Unduna wa Maphunziro udalengeza kuti ophunzira asamalipire fizi komanso K500 yochitira zitukuko…

Leather SMEs want govt to stop importing police boots

Small and medium enterprises (SMEs) in the leather sector have asked the government to stop imports of police shoes so that manufacturers can produce them locally. The players said the government would save forex used to import the shoes. The SMEs expressed the sentiments after undergoing a Malawi Enterprise Productivity Enhancement (Mepe) eight-day footwear designing…

Ref speaks out on Airtel Top 8 final

  Referee Micheck Juba who officiated the Airtel Top 8 final between Nyasa Big Bullets and Blue Eagles which was marred by violence, has come out of his shell to defend his decision to award Eagles a late penalty. Juba was physically confronted by Bullets fans and players after the match for awarding Eagles a…

Kamuzu Stadium gets fresh deadline

  Government and contractors responsible for Kamuzu Stadium renovations in Blantyre have set July 30 as a deadline to have the works completed and hand over the facility to the Ministry of Labour, Youth, Sports and Manpower Development. This follows a visit to the stadium by the ministry’s director of sports Jameson Ndalama yesterday which…

La 40 lakwana kwa womata anthu phula

Wakhala akumata anthu phula m’midzi kuti amupatse ndalama ndipo adzakhala ndi mwayi wopeza ngongole kuchokera ku bungwe la Emmanuel International. Midzi 21 ya kwa gulupu Makumba ndi Mtaka ikulirira ku utsi atawakwangwanula ndalama dzuwa lili gee! La 40 lamukwanira Wyson Mandolo wa zaka 36 pamene bwalo la milandu m’boma la Mangochi lamupeza wolakwa ndipo akukaseweza…

‘Zovota ife ayi’

“Anthu opotsa 3 000 adalembetsa unzika m’dera langa. Lero anthu 1 240 okha ndiwo alembetsa kalembera wa zisankho.” Izi ndizo zachitika m’dera la mfumu Chilowamatambe ku Kasungu komwe bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) limachititsa kalembera wa zisankho moti likapanda kubwererako, anthu ambiri sadzavota nawo m’bomalo pa zisankho zapatatu za chaka cha mawa. “Anthu akuti…

Kampeni yayamba ndi ukali

DPP ithamangitsa otsutsa ku Thyolo Kumeneko ndi kunyumba kwa APM—Chakale Kwa eni kulibe mkuwe. Mdima udadza masanasana m’boma la Thyolo pamene gulu la Chilima Movement lidalephera kuchititsa msonkhano wake nkhondo ya mawu itabuka ndi otsatira chipani cha DPP. Wachiwiri kwa mlembi wa DPP, Zelia Chakale, adati gulu la Chilima Movement lidachita kuishosha dala chifukwa limafuna…

Kalembera wa zisankho ali mkati

Dzuwa salozerana, kalembera wa zisankho udayamba Lachiwiri m’maboma a Dedza, Salima ndi Kasungu. Izitu zikudza pokonzekera chisankho cha makhansala, aphungu a Nyumba ya Malamulo ndi mtsogoleri wa dziko lino chomwe chidzachitike mu May chaka chamawa. Aliyense ali ndi mwayi wodzavota akalembetsa. Kutanthauza kuti ngati munthu salembetsa, sadzapeza mwayi wodzaponya nawo mavoti. Komishona wa bungwe loyendetsa…

Gulewamkulu, agumula sitolo

Gulewamkulu wina Lachwiri lapitalo akumukayikira kuti adagumula sitolo ina pamsika wa Nkhalambayasamba m’boma la Mchinji ndipo akumukaikira kuti adasakaza katundu wa K3.5 miliyoni. Mneneri wapolisiyo, Kaitano Lubrino, Lachisanu adati apolisi amanga anthu 16 amene akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi nkhaniyo. “Anthu onsewa tikuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi zophwanya sitoloyo komanso kuba katundu,” adatero Lubrino. Malinga ndi Lubrino,…

Milk wastage to drop

The country will start registering a drop in milk wastage following the opening of K1.5 billion milk collecting centre and cooling plant by Lilongwe Dairy Limited at Goliati in Thyolo. Over the years, milk wastage has been a key issue for bulking groups due to unpredictable power supply and poor maintenance of collecting plants. The…

Mangani womenya wotsatira MCP

Chipani chotsutsa cha MCP chapempha apolisi kuti aponye m’chitokosi Isaac Jomo Osman, kadeti wa DPP amene adasautsa ndi kuvulitsa mnyamata amene adavala malaya a chipani chotsutsacho. Lachiwiri m’sabatayi, Osman, yemwe adakhalapo wapampando wa masapota a Big Bullets, adajambulidwa akulamula mnyamatayo amene adavala malaya a makaka a MCP kuti ‘avule ndipo asadzayerekeze kuvala makakawo.’ Izi zidachitika…