Chichewa
-
Anatchezera
Za Chikondi ndi chibwenziAgogo,Kodi chibwenzi ndi chikondi ndi zosiyana bwanji? Mwina funso limeneli likhoza kuoneka ngati lopanda nzeru koma kwa…
Read More » -
‘Yunifolomu ya polisi idamukhala’
Padali pa 14 June 2017 pomwe Richard Chitsamba adamuona koyamba mkazi wake Fosina Vasulu. Apa nkuti awiriwo akuweruka m’zintchito mwawo…
Read More » -
Amapita kukagula zomwera tiyi
Kukumana kwanga ndi mkazi wanga kudali koseketsa kwambiri chifukwa ndidakuna naye akupita kukagula shuga ku golosale komanso zomwera tiyi,” adalongosola…
Read More » -
Anatchezera
Takulandiraninso mu 2021 Ndikufuna ndikulandireni m’chaka cha 2021. Chaka chatha lidali thumba la zambiri. M’chakachi zina zidali zokoma, koma zina…
Read More » -
Odzipha akuchuluka
M’chaka cha 2020 chiwerengero cha anthu odzipha chidakwera poyerekeza ndi cha m’chaka cha 2019. Kafukufuku wa apolisi akuonetsa ku chiwerengerochi…
Read More » -
Mbuzi ndi zosavuta Kusamalira, kudyetsa
Mlangizi wa ziweto wa ku G&LM Vet Services, Edwin Nyondo, wapempha alimi ambuzi kuti aziika mtima pa ulimiwu kuti azipeza…
Read More »