• Nkhani

    Amuna anga matama thooo!

    Azakhali, zili kwathu simungazimvetse. Ife tonse tili pa ntchito. Tonse timalandira ndalama zokwanira ndithu. Komwe ndalama za amuna anga zimapita…

    Read More »
  • Nkhani

    Ati tikhwimire mwana

    Ndili pa banja ndipo tili ndi ana angapo. Banja lathu ndi loopa Mulungu. Ndipo tonse ndi atsogoleri ku mpingo wathu.…

    Read More »
  • Nkhani

    Ndimamufuna kwambiri

    Anatchereza M’mudzi mwathu mudabwera mtsikana wina wake yemwe ndidakondweretsedwa naye. Ndidachita machawi kumufunsila ndi kumuuza kuti ndimamukonda koma sadandiyankhe. Mwa…

    Read More »
  • Nkhani

    Ndalama zawo sizikulondeka

    Zikomo, Anatche, ine zandivuta koopsa. Ndili pa banja ndipo ndili ndi ana atatu. Banja lathu ndi losalongosoka. Ndanena chonchi chifukwa…

    Read More »
  • Anatchereza

     Kodi nditani? Gogo Natchereza Ndine mtsikana wa zaka 25 ndipo ndakhala pa chibwenzi ndi mnyamata wina kwa zaka zinayi. Mnyamatayu…

    Read More »
Back to top button