Chichewa
-
Covid-19 yakolera
Chiwerengero cha Amalawi amene apezeka ndi kachirombo ka coronavirus chatumphuka m’sabata ikuthayi kuchoka pa 101 kufika pa 203. Izi zachitika…
Read More » -
Mkokemkoke patsiku la chisankho
Zipani zotsutsa boma zalembera bwalo la milandu la Supreme Court kuti lifotokoze bwino pa za yemwe akuyenera kusankha tsiku loti…
Read More » -
APM alola ansah achoke
Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika dzulo wavomereza kuti wapampando wa bungwe la zisankho la Electoral Commission (MEC) Jane Ansah…
Read More » -
Chipwirikiti pachisankho
Pali chipwirikiti pachisankho cha mtsogoleri wa dziko lino, pomwe wapampando wa bungwe la zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane…
Read More » -
Andale agundika misonkhano, osapewa Covid-19
M’sabatayi, anthu ena 5 adapezeka ndi kachirombo ka coronavirus m’dziko muno, kuchititsa kuti chiwerengero cha anthuwo chifike pa 63. Chiopsezo…
Read More » -
Chisankho chiliko
Bwalo lalikulu la milandu la Supreme Court dzulo lidagamula kuti bwalo lapadera la Constitutional Court (ConCourt) silidalakwe pogamula kuti chisankho…
Read More » -
Teketeke popereka zikalata
Mzinda wa Blantyre mudali teketeke m’sabatayi pomwe bungwe la zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lidalandira zikalata za omwe akufuna…
Read More » -
Anatchezera
Sakufuna kukaonekera Gogo Natchereza, Mnyamata wina adandifunsira chibwenzi ndi cholinga choti tidzakwatirane. Padakali pano padutsa zaka zinayi tili paubwenzi, koma…
Read More » -
‘Adatuma nthenga kudzandifunsira’
Kudali ku Dedza, mwezi wa October m’chaka cha 2017 pomwe Lucy Mvula adalandira uthenga kuchokera kwa mzake wa Geoffrey Kishombe.…
Read More » -
Pimani onyamula mafuta
Kati deru kadaopsa mlenje. Anthu okhala kwa Sonda komwe kuli nkhokwe za mafuta m’zinda wa Mzuzu sakumwa madzi ndi madalaivala…
Read More »