Chichewa
-
Alimbikitsa chitetezo cha okhala m’malire Covid-19
Bungwe la Farmers Union of Malawi (FUM) lati pakufunika kulimbikitsa chitetezo cha anthu m’madera akumidzi omwe ali m’malire a dziko…
Read More » -
‘Pewani chukwu Ku mtedza’
Chukwu kapena aflatoxin m’Chingerezi ndi liwu lomwe silichoka pakamwa ku ulimi wa mtedza m’dziko muno chifukwa ndi chipsinjo chachikulu ku…
Read More » -
Mtambo walowa ndale
Yemwe adali wapampando wa gulu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) Timothy Mtambo wati wasintha nthabwa ndipo pano wayamba ndale…
Read More » -
Apha mkazi wake kaamba ka nsanje
Akuluakulu amati pali nsanje pali chikondi, koma zina zinyanya. Nsanje zina zimaonjeza ndipo zimasanduka chiopsezo pa miyoyo ya anthu ena.…
Read More » -
Woyendetsa ambulansi ataledzera amangidwa
Dalaivala wa ambulansi ya pachipatala cha boma cha Chiradzulu zake zada atagwetsa galimotoyo m’ngalande chifukwa choledzera. Malinga ndi kanema imene…
Read More » -
MCP, UTM asainira mgwirizano
Kudali khwimbi la anthu ku Kamuzu Institute for Sports ku Lilongwe Lachinayi pomwe zipani zotsutsa zimasayinira mgwirizano wawo motsogozedwa ndi…
Read More » -
Mutharika asosola nthenga atsogoleri
….asankha nduna, koma Chimunthu Banda aukana Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika sabata imene ikuthayi anali wotangwanika zedi chifukwa ndiye…
Read More » -
Njovu ziwiri zitengetsana pa 19 May
Zadziwika tsopano kuti njovu ziwiri zomwe ndi mgwirizano wa Democratic Progressive Party (DPP) ndi United Democratic Front (UDF) komanso Malawi…
Read More » -
Chisankho chipitirire—bwalo
….Khoti lalikulu likana pempho la MEC Bwalo lalikulu la milandu la Supreme Court Lachinayi lidakana pempho la bungwe la zisankho…
Read More » -
Mtsutso pa masiku a chisankho
Mtsutso wabuka pa za masiku a chisankho cha mtsogoleri wa dziko lino chomwe chikuyembezeka kuchitika pa May 19 chaka chino.…
Read More »