Chichewa
-
Kota yatha, JC yabwerera
Unduna wa za maphunziro wathetsa njira yosankhira ophunzira m’sukulu zaukachenjede yotchedwa kota, komanso yabwezeretsa mayeso a JC m’sukulu za sekondale.…
Read More » -
Aphungu akumana Lolemba
Pamene aphungu ayambe kukumana Lolemba posanthula ndondomeko ya pakati pa chaka ya momwe boma lagwiritsira ntchito chuma, sipikala wa Nyumba…
Read More » -
Apempha MEC iyalule mphasa
Bungwe la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) lati potsatira chigamulo cha khoti kuti bungwe la zisankho la Malawi Electoral Commission…
Read More » -
‘Chilungamo cha pakati pa usiku ayi’
Gulu la za maufulu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) lati nthambi yoona za makhoti komanso bungwe la oimira ena…
Read More » -
Apolisi sakununkha kanthu pa chitetezo
Ng’ombe zayang’ana kudazibomu! Ubale wa anthu ndi apolisi wafika pa wa mphaka ndi galu moti apolisi sakununkhanso kanthu pa ntchito…
Read More » -
Atsogoleri a ndale akuona 2020 owala
Atsogoleri a zipani za ndale zomwe zidalimbana kwambiri pachisankho cha pa May 21 2019 ati akuona chaka chowala cha 2020…
Read More » -
2019 Polisi Idaziona
M’chaka changothachi cha 2019, nthambi ya chitetezo ya polisi idalibe mpata opumira chifukwa cha mpungwepungwe womwe udalipo ndikusukuluka kwa chikhulupiliro…
Read More » -
2019: Chaka cha mbiri pa zisankho
Chaka cha 2019 chidzalowa m’mbiri ya dziko la Malawi ngati chaka chomwe atsogoleri azipani adakwekwetsana koopsa komanso koyamba mukhoti pankhani…
Read More » -
Amalawi adalankhula kudzera m’zionetsero
M’chaka chomwe chikuthachi, Amalawi adamasula thumba la ukali wawo nkulankhula mokwenza makamaka pofuna kuwonetsa kuti adazindikira za ufulu ndi udindo…
Read More » -
Mipingo yadzudzula nkhanza
Atsogoleri a mipingo ati nkhanza makamaka zochitira ana ndi amayi zanyanya m’dziko muno moti asungwana 21 pa 100 aliwonse komanso…
Read More »